Email a copy of 'Malawi opposition raises concerns over death threats: ‘Stop being critical to President or you will die’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi opposition raises concerns over death threats: ‘Stop being critical to President or you will die’' to a friend
Blue Eagles Sisters send a warning signal in the Central Health Lilongwe and District Netball League on Saturday as they...
Trying to intimidate people in opposition is not a solutIon malawians want to hear.malawians want tangible solutions from the multiple problems they face by their government.assassinations of those officials is plain stupid and dangerous.the backlash from that could see you,the perpetrators,a mass-hunt by the populace to kill you too.Solve the damn problems,no threats!
Ngati Boma Likudana Ndi Kudzudzulidwa Ndiye Kuti Anthu Amene Akuyendetsa Boma Sakudziwa Kuti Democrancey Ndi Chani, Mmenemu Ndi Mmene Dziko La Democrace Limayendera, Or Muphe Anthuwa Dziwani Ndithu Kuti One Day Mudzakhala Kunja Kwa Boma, Sindinu Amuyaya Ayi, Yendetsani Dziko Ndi Chikondi, A Opposition Mutawamvera Zomwe Amanena, Mutha Kuchita Bwino Ngati Momwe Anachitira Bwino Malemu Bingu Mu Zaka Five Zoyambirira Zija, Anayigwiritsa Ntchito Opposition,
come what may, forces will force matters
lets shame the devil.say no to demo
say no to suffering
say no to madeya, love nsima
say no to treason
say no to groaning
pray to God for help
He become concerned when the children are suffering. exodus 2 :23
he become attentive to the cry of the isralites.
is Malawi genuinely crying?
lets turn to God
God will fight your battles
God Bless Malawi and its leaders, be it in power or in opposition
Peter akupha wa opposition lizamuweluza ndi dziko lonse la pansi chifwa alindiasilikili ndiponso police , chiweluzo chake ndi kunja kwa Malawi ndiye achenjere ndiponso awone kusiyana kwache , zimene akupangazi ndimasewera. Wachepa Peter opposition itha kumugonjetsa ndi kachipani kache ka 34% .
mbuzi iwe osangozisiya bwnj….. zimafuna olimba mtima izi osat kukamwa ngat wapana mwanaliye choncho
dpp is a party of thugs, they are still thugs and will remain thugs!!!!!!
DPP is a helpless and clueless party. No wonder they are threating lives of opposition leaders because they are new to Malawi – they never fought for freedom during early 90s. they are there to enrich themselves and not serving the interest of Malawians. They did not win 2014 but rose to power through head of electoral commission and not by votes. 2014 was a rigged election even children know this – why did a big person weep during announcement of the winner, he knew he had betrayed innocent Malawians.
“Mwamuna mzako m’pachulu n’kulinga utakwelapo” Agalu inu a DPP muyerekeze kuchita zamanyi zanuzo, chimunthu chanu chopanda mano nkamwacho chidzagwa ngati nkulu wake uja, fotsekiiiiiiii !!!!!!!
How many have so far died out of these so called death threats?
Every office has its own challenges, don’t you know?
You are calling the president to step down. Do you think that those who voted for him can just leave you like that?
Zimatiwawatu kwambiri, kapena simunamveko kuwawa kwake eti?
Yesetsani campaign, mukadzawina zisankho a PP kapena MCP mudzamveko kuwawa kwake anthu amene sanavotere Chakwera akumuwuza kuti atule pansi udindo.
Inuyo amene mwavutikira kumuvotera tiwone ngati mudzangokhala duu.
Enanu tidzaka titatu tapitatu munasauka nkumavala timajinzi tothina mtaunimu anthu kumati kodi ndi auje awo mukuyenda khwekhwelekhwekhwele zitakusokonekelani…pompano musaukanso muwona…munasakha game yachabe…mukulimbana ndi Kabwila munthu wophunzila bwino osati kuphunzila kongogulanazo mapepala…kumangolankhula english yoloweza basi…tima vocabulary toloweza basi…zaziii…ine mjomba ndisazakuoneni muli deludelu kulowela kunyumba ya Kabwila kuti akupelekezeni kwa Bigman Chakwela kuti akakupepetseleni mutavalanso kajinzi kothina…