Email a copy of 'Malawi Police arrest pair ‘caught during sex act in car’ at Kamba' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police arrest pair ‘caught during sex act in car’ at Kamba' to a friend
State House is accusing main opposition Malawi Congress Party (MCP) of working out of frustration to disturb President Peter Mutharika...
why caught these people. to do sex in the car is it bad
Police beta find ava tings to du.. is this a crime
??
mukuleka kugwila mbava zoba ndalama zabomazi mukulimbana ndi anthu oti amazithandiza okha mmati ngati ya room alibe asathandizane kuopa police?
Sectetion imeneyo 180 ichoke yaphelana ufulu. pemphe akulu wosamaila kondomu.
Influence of liquor.but why people?
Malawi, Malawi, Malawi…………………..malawiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
Apolisi mukanangowaza kuti Kabisale osati kumanga.sex palibe wolesa
Dziko lathu ili lafika poola. Anthu kufikana pomyoza a Police chiifukwa choti agwira Anthu akuchita chigololo malo asayenera.Eeee, komanso Kubweraku ai zafika penapake. Titati tipange kafukufuku wa Anthu amene akugwirizana ndi zimenezi tipeza kuti 95% ndi a Kumwera.Ngati agalu paliponse.
Let Us Be Spiritual.Malawi Need God’s Intervention.This Things Need To End.Every1 Must Take Action To Stop This.Lets Us Pray That God Shd Change Us.Police Officers Had To Arrest Them In Respective Of Their Job.
Dziko lapansi likuthatu apa! mpaka making love at such public place? inunso a police kupanda manyazi kumalimbana ndi nkhani zopusa ngati zimenezo? inunsotu mumatero mu ma offices anu koma kwakula ndi kusagwidwa! zopanda mcheretu izi!!