Email a copy of 'Malawi Police arrest two for running illegal clinics' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police arrest two for running illegal clinics' to a friend
Basketball Association of Malawi (Basmal) has a new committee following low key elections held on the sidelines of an Annual...
Slap them with harsh punishment, chichewa chake amati IHL (Imprisonment with Hard Labour). Anthu opanda chisoni, kumaba mankhwala iwo nkumakagulitsa. Not good, bu hau!!!!!
Apolisi afufuze komwe anthuwa amakatenga mankhwala a boma. Tikudandaula kuti ku zipatala kulibe mankhwala pomwe anthu ena oyipa mtima akumagulitsa mankhwala.
amasuleni anthuwa kodi umbava mwaona wamankhwalawu basi?bwanji osamanga Joyce Banda ndi mbava nzakeyu Peter Muthalika omwe aba chuma cha bomawa .Amasuleni madala angawo zinthu zisanafike povuta mwamva?Nanunso a Aubrey Norman mutu wanu ukugwila mukuti alandile strong charges ife tizikadya pakhomo pa amayi anu?
Little motivation agitated people to stealing
Apolice nsanje, anzanu asatakate pa town? They r jst trying to earn a leaving, no job pa nyasaland. Let them go!
It is obvious that there are NO operational systems in place to stem this behaviour. Free for all starts from the top…what do you expect?
Anthuwo ankagwira ntchito kuchipatalako or wat? A good reporting should’ve considered that,coz how dd they get zipangizo za boma!
Those people must recieve strong charges because they are making people to get problems in our Hospitals while they are steeling Medicine,Osalekelera ndiwomwewo akumafalitsa kuti Boma ikulephela kukwanilitsa zomwe inalonjeza mankhwala akusowa nzipatala, Anthu akumwalira ndinchitidwe ngati umenewu.
Interestingly DHOs will make a lot of noise that hospitals are under funded hence difficult to manage but you will be baffled to see that there is gross misuse of the little resources available.
Mukuti zipangizo kulibe muzipatala while others are running dodgy clinics in other places.The very same people who work in govt hospitals are the one selling govt medical stuff to some unlicensed private hospitals.Katangale wavuta pa Malawi.