Email a copy of 'Malawi Police block supporters of opposition leader at airport: MCP condemn action' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
zeus
6 years ago

Dziko lamalawi likufunika munthu owoopa mulungu zithu sidzilibwino chinyengo chachuluka boma mu

zax
zax
6 years ago

KUTENGA BOMA SICHINTHU CHAPAFUPI AYI,MCP KUTI IWINE IYENERA KUCHILIMIKA CAMPAIN DZIKO LONSE OSATI CHIGAWO CHAPAKATI CHOKHA AYI…..CHIPANI CHANJI KU NEC EVEN MSILAMU KULIBE CRNTRAL REGION YOKHAYOKHA sorry

joseph malanga
joseph malanga
6 years ago

Makomentiwa osamangowale musanamvetsele bwino nkhani.Achakwela amayendela za mpingo n amayenera kupezakako ku airtport analinso ampingo not party members.mukamati bwana 2019 muwina mukunamizana mmbwereza kuonatsa mwano mcp sidzawinanso kupha,kumangana nyakula,munawadulitsa makadi awiri alongo anga Ali oyembekezeala nkhaza Zambiri sitinganene

dabwani zoona
dabwani zoona
6 years ago

Air Port is.not a place for political rallys.The place is a busy travel pkace so Chakwera was wrong.

Zudi Mzee
6 years ago

Kodi a DPP bwana Chakwera anakulakwilani chani. You fight him everyday instead using misonkho yathu kutigulira mankhwala muzipatala. God, please in 2019 help us to remove this leadership we are tired of this corrupt leadership.

ovaha mbwiyanga
ovaha mbwiyanga
6 years ago

Ambuye one leader at a time. Ngakhale ku mpingo ndi choncho. Chakwera and chipani cha magazi that cheap politics. Inutu musanati mumva mbebe….. Bwelerani ku mpingo baba ndale simungazithe

zako izo
zako izo
6 years ago

Chakwera ndi a Galatiya uyu anayamba ndi za mulungu pano akusilizira ndi za m’dziko azako amayamba ndi za m’dziko kusilizira ndizamulungu lero musadandaule zam’dziko ndiye zimenezo

Truth shall prevail
Truth shall prevail
6 years ago

The most incompetent and corrupt police in SADC region.

nyoni
nyoni
6 years ago

anthu amene anayera kupezeka kumeneko ndi a church not mcp supporters,since the singapole trip was

a church trip

Mzozodo
Mzozodo
6 years ago
Reply to  nyoni

KKkkkkkk, that makes sense

Neutral Poliician
Neutral Poliician
6 years ago

Those supporting Chakwera’s intention to be welcomed at the Airport must be sick in your head resulting into your sick thinking and expectation. You can’t expect just a mere opposition leader to be emulating the practices or honour accorded to a Head of State. Mukupopa munthu to be dressed in borrowed robes. God willing, Chakwera must wait for his time. Komanso a Chakwera nanunso penapake you don’t seem like an educated kapena a former man of God. Can you really be serious nkumaona zopusazo inu mukuona nkumayembekezera zopusazo? Don’t disappoint us. Kenaka muziti ndife a MCP owukila pamene we jus… Read more »

Read previous post:
Malawi Queens date Botswana in friendly game

Malawi national netball team, the Queens will host Botswana in preparation for the 2o18 Gold Coast Commonwealth Games to be...

Close