Email a copy of 'Malawi Police shake up Chilobwe station: IG cautions 'bad apples'' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Police shake up Chilobwe station: IG cautions 'bad apples'' to a friend
Local human rights activist, Voice Mhone, who was appointed Malawi's Ambassador-designate to Germany, has given government seven days to tell...
Ine ndiye ndimachoka kuchinkhoswe ndinapeza road block mmalo mopanga zantchito anafunsa kuti mulu ndi mmodzi green,ine ndinangoti eko anveke aya tikunkhe kukhosi.Zantchito mulibe amenewa amangofuna ndalama pa mseu.
Mr IG I was in Karonga last week and in the evening I decided to go and eat at a restaurant called Maharaj . While I was waiting to get my food, three officers in full police uniform came in totally drunk. One officer started vomiting in the presence of patrons. His colleagues removed his uniform and gave him a red Tshirt which was for a civilian friend (Rasta). The police hat was all dirt as it was being tossed from one end to the floor. You may cross check my story with the waiters , as it was such… Read more »
Muonenso magalimoto omwe amayenda msewu wa Midima makamaka ma minibus. Ambiri amakhala opanda misonkho koma chifukwa amadziwana ndi a Police a pa Bangwe. Tngoganizani minibus kudutsa pa Bangwe ndi kukagwidwa pena pomwe pali a Police. Pali zabwino apa? Magalimoto ambiri amangodutsa osaonedwa koma kumangochedwetsa anthu oti akuthamangira ma emergency. Pa Bangwe Police alinso pa mtambasale. Muunike bwino.
Rotten police nanu tidzikuotchani
The IG should also look at corrupt Traffic officers , Blantyre Police . most corrupted. Dunduzu road Broke , my God.Up to now Sitting capacity for for Mini bus from Mzuzu Depot to Karonga is four Passengers, why . They just corrupt a police officer at Dunduzu Road broke.
the criminals chose Guta because they Knew his criminal record. The operation was being done in Limbe and why didnt he inform Limbe police. he should face the music.He snatched somebodys wife inticing her with blood money gotten from his criminal activities. We need new officer to stop the noisy touting. Even Ntonga should stop subleasing his plot for the sharks taking shape at Chilobwe Centre where satchets are being sold. All police officers residing in chilobwe should be moved away.
Mrs F. MAKILENI NDI WAKUBA KWAMBIRI PA KILOJNGWE POLICE. HOW SHE GOT SELECTED FOR PEACE KEEPING AFTER FAILING INTERVIEWS WE DONT KNOW. AKABA NDI MBAMVA AMAPATSAKO MA BWANA
Ananyanya apolisi a pa Chilobwe, ngakhale chakudya cha munthu wosekeredwa, chomwe abale ake ambweretsela, ngati ndiwo ziri zankhuli amadyamo nkungosiyamo nsudzi okha. Mchiyankhulo chawo amati kusodola! IG ayang’anenso apolisi a pa boma pa Nsanje. Apolisi a pa msewu nawonso ndi okuba zedi!
A lG ,muchepese kuzola calorite.kumaso ngati kwa khanda.
Even in Euthini there plenty guns of which owners dont know how to use them.Some brought them in beerholes chasing pple like dogs at the presence of police officers,