Email a copy of 'Malawi President’s defamation claims: Kaliwo representing Ntata, Nyasa Times to name legal team this week' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

46 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
clement
clement
8 years ago

Nkhwangwala wa mantha adafa ndi ukalamba

Vwapuvwapu
Vwapuvwapu
8 years ago

The battlefield (court) is ready, kkkkkk.

clement
clement
8 years ago

This Ntata has nothing to do that’s why he is trying to spoil the image of the president but he will cry now now just wait. You’re competing with head of state chosen by people so the same people who loves the president will hit you.

chingolopiyo
chingolopiyo
8 years ago

Kunena kwa ndithendithe Nathabwe anadzitengera. Ng’oma yolira sichedwa kusweka. Ukayenda kumasiya phazi, ukasiya mulomo uzakupeza. Ntata, I can see that you have started sweating even at -18 degrees. TInkanena adathira mu siizi. Mawu akulu akoma akagonera mwanawe. Chosamva adachiphikira masamba, Ntata. Good luck!

levelheaded
8 years ago

My advice to mtata. Ayise ife tatopa ndikuwona infa za dzidzidzi za achichepere a size yakoyo. Ndiye poti unaziyamba kale ife ndiomangomva zothaitha. Ukayiwina nkhondo imeneyi mwina ukhala oyamba poti tawona anzako ambiri omwe anafa Ali makanda chifukwa cholimbana ndi boma. Ukaphedwa sadziwika amend wakupha anthu amangoti linamupha ndi boma. Dziwa kuti ndizachikale zomati anafera dziko ndipo zinapita ndi john chilembwe masiku ano anthu akuganiza za ana,banja ndi achibale. Penapake president atha kunena kuti mu ulamuliro wanga sindikufuna kukhetsa mwazi koma pena zochita ngati zakozo zofuna kuti udzigwira ntchito ya ma khoti ndizimene zimapangitsa president kuti aphe ndithu chifukwa amati… Read more »

ndege
ndege
8 years ago

Mawa ndiyimba

sapitwa
sapitwa
8 years ago

Bwinotu bwino. Wina atsowa!

nachisale
nachisale
8 years ago

Ngati pitala sanabe ndiye akuletseranj Ntata ndi nyasatimes kuti asamazindikizenso zokhunza MK92, ndiye kuzigwiritsako, tiye nazo Allan Ntata ulula ayaluke, alomwe okubawa

Kenkkk
Kenkkk
8 years ago

We don’t want anyone to be killed or eliminated before and during the court hearing time. Ntata camp be careful security-wise.

I expect a u turn from the president. He is treading on a very hot coal pathway.

GooNgayikosya
GooNgayikosya
8 years ago

hayi!!! hamumkoka nditogona ndi mwana amayeee!!! Mtata tiyemoni mbuyache

Read previous post:
Malawi regroup for Tanzania tie in World Cup qualifiers

The Malawi national football team aka the Flames regrouped on Monday in readiness for the 2018 World Cup preliminary qualifiers...

Close