Email a copy of 'Malawi prison boss shoots dead two sons, arrested: 5 nabbed for cop’s murder' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

200 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
che chipojola olowesa jando kwangonji .
che chipojola olowesa jando kwangonji .
9 years ago

Eeeeeeeish awatu ndiye achachanda, ndipo ndiye alindi chandamale, samaphonya, take cover,komaso mumufufuze ameneyu ngati wachitira izi mikozo yake yomwe , kulibwanji akaidi waphatu phwiiii .

TOLITOLI
TOLITOLI
9 years ago

I Support The Father.Ana Anamutopesa AWa
Could Nat Be The First Time

Francisco Mkozomba
Francisco Mkozomba
9 years ago

Achita bwino kuwapha apuludzu amenewa, ana amwano, makani, nkhwidzi,osamva,uhule
Zamwano mnyumba mwa makolo basi! Iyaa! Ndiponso akanamupha ndi Lusungu wamkazi
Yemweyo,aaa! Ana ochita kutopetsa chonchi? Ndiye ana mpaka kumera dzindevu koma kumakhala ndi makolo awo, bwanji osakwatira? Usilu basi! Makolo enanso muchenjere zilombo mukusunga mnyumba mwanuzo! Koma 2015 kuli zinthu!

Criticalmind
Criticalmind
9 years ago

It aint an easy thing to stay with parents when your a grown and doing nothing so the best thing is to use your charnces while still young…so that atleast you should have something to do in future.

Alex
Alex
9 years ago

Azibambo aulesi osagwira ntchito koma kulawirila kukangana basi,ana opusa akuyenera kufa ndithu 29-23 alibe m’manjamwamakolo ana opusa ause muntendere.wokuphayo alagidwe molingana ndimalamulo wokhudza kupha.

Naphurwe wa Mmainje
Naphurwe wa Mmainje
9 years ago

Poor Chisi, why? However Pliz understand this old man. Makosanawa anakula ndipo amasowetsa mtendere.

Dj Thomzy
9 years ago

This aint fair

Yamikani
Yamikani
9 years ago

Akuluakula amenewo mukafufuza mutsyre madalawo, anatopa nawo anawo.

Eliam k
Eliam k
9 years ago

Lesson to unruly children,at twenty something kumakhalabe ndi makolo,wina yonso akuti anangosiya ntchito ku prison why?madalawo ofunika bail,my opinion

Aaron mwansambo
Aaron mwansambo
9 years ago

Akuyenera kulandira chilango basi,vutoli analilekerera poyamba

Read previous post:
Airtel testifies Kumwembe, Pika were in Malawi before and after Mphwiyo’s shooting

Mobile telecommunications operator Airtel Malawi gave testimony in the shooting of former budget director in the Ministry of Finance Paul...

Close