Email a copy of 'Malawi Queens need K15m for World Netball Series' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Queens need K15m for World Netball Series' to a friend
Malawi currency the Kwacha continue to face a slide against the major world currencies with opposition parties saying its worrying...
If u change the name to Mulli Netball team a cheque of 1 Billion will be given to you.
chonde chonde atsikanawa apaseni 50 million inayao agawane ndithu iyi ndiye team osati chamendo chitimu chochimwitsa ngati chimenecho mukapanda kwapasa tilowa munseu ndithu
Give them not football national team our neetbal national the put us on the map
Tengani allocation ya Flames apatseni atsikana akatitukulire dziko!
They should build these guys a world class netball arena rather than burning money into Flames !!!
Let no one say there is no money. Give them quickly and double it. Use the fastest means of releasing the money. Legally. No red tapes here. They always use it to good cause. They deserve no “buts”.
AKUPASENI NDALAMAZO BASI NDIPOSO OSATI 15 YOKHA IKHALE 25 CHIFUKWA NETBALL NDIIMENE IMATICHOSA MANYAZI, OSATI KUPITA KU ALGERIA KUONONGA 36 MILLION KUKACHINYIDWAKO 3 KWA O ZACHAMBA BASI. NO MORE NATIONAL FOOTBALL TEAM BUDGET ATITOPESA NKULUZA. INU ABOMA THIS TIME MUKANGOIPASA FLAMES NDALAMA NDIDANA NANU..
Iyi ndiye Team yoti muithandize osati mpira wa mapaziwo
Apa ndiye bola,osati zinazi ayi.
Iyi ndiye team yoyenera kuithandiza mosawinya osati zijazi.Fundraising dinner and dance pa COM bwa?