inu ndiye mwayitha chemwa mwapeza kasinkhu wanu ndithu osati a Tina anapeza nzungu okugwa ndikumina ati kufela ndalama munthu othaitha kale ameneuja shame on you TINA
Kulinda Mtere
9 years ago
Ayise Masa, washosha dala mwali wa fitness ya kathithitu. Nde nawenso ofunika uyambe gym. Nanga lobodolobo akuoneka mu jacket yo akuthandiza?
Samson
9 years ago
I find this to be in order!
Mbolo Sidwala
9 years ago
Chitsanzo koma chimenechi, osati tinazimva last week! Anthu amalowa m’banja ali ndi mwana kale, munthu wa Mulungu nkumati mukhale chitsanzo kwa anzanu. Meaning what?
Chikopa
9 years ago
Zabwino zonse kumakondana osati kumenyana paja anyamata amasiku ano chamba
inu ndiye mwayitha chemwa mwapeza kasinkhu wanu ndithu osati a Tina anapeza nzungu okugwa ndikumina ati kufela ndalama munthu othaitha kale ameneuja shame on you TINA
Ayise Masa, washosha dala mwali wa fitness ya kathithitu. Nde nawenso ofunika uyambe gym. Nanga lobodolobo akuoneka mu jacket yo akuthandiza?
I find this to be in order!
Chitsanzo koma chimenechi, osati tinazimva last week! Anthu amalowa m’banja ali ndi mwana kale, munthu wa Mulungu nkumati mukhale chitsanzo kwa anzanu. Meaning what?
Zabwino zonse kumakondana osati kumenyana paja anyamata amasiku ano chamba
Bolatu uyu osati aja anangotola mzungu wothayitha aja.
I seem to know the gentleman on the far right. He is a clinician. It was great indeed.
comgrats Bayano n Towera nzabwinotu izi mwachokera patali guys
Kaya zanu izo. Ife ndiye tili Ku lake of stars
Bwino mukasamalane osati muziti yaviyavi ndi vidya makanda vamatenda mumpake nyamatamata ngati ameneyo. thats good wakwakwaza kanyamatatu osamakomedwa ngi khusa ngati zinzzija