Email a copy of 'Malawi recalls diplomat Brigadier Chirwa from Kenya' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi recalls diplomat Brigadier Chirwa from Kenya' to a friend
President Peter Mutharika has asked the international community to ignore or shut their “unsuspecting” ears to a politician who is...
Iwe Oluza ndiwe mbuzi, hope u wrote ur commeng under the influence of weed and sachets hangover. Chirwas are tonga, dont display ur stupidity here, ignoramus begot
Ndale zokokana our country will never develop. Be mature good people. Love your country.
he went there because of politics and he is coming back because of the same politics«« pimpa
Abwere basi ,ena apiteko , palibepo nkhani apa , kodi ikhale nkhani chifukwa ndi mbwenumbwenu,nanga ena anzigawo zinazi abwerawa bwanji inu atumbuka simumanena kathu.
Azibwela basi palibe chodabwitsa onse abwelawa iyeyo ndiye wopambana?
A malawi kodi amene mukunyoza ndi kusangalala mawa zinthu zikamazasintanso musazanene kuti akukondela or against alomwe or south be aware ndi mawa ngati ndipathali posachedwapa malawi asintha mulungu atiyanka, remember ndi mawa.
Ya over 200 cars ibwera liti
Nanga mabvuto tiri nawowa akhonza liti?
Mavuto ake ngati chiyani. Just mention them. I will come back to you. Iam waiting
Abwere poti boma lalamula,koma sibwino kusitha maudindo anyhow.pali yositha maudindo vuto si APM koma system yathu
Watsala Capricorn (Reuben Ngwenya) amene anapangitsa kuti ma Brigadier ndi General anamangidwawo kuti akalowe ku Maula. Mbuya Chinauluka, chinatelemuka. Unaona ngati anjako ndi phenembe? Wa, walonganji mphale?