Email a copy of 'Malawi Revenue Authority impounds 42 kilos of Indian hemp in Mzimba' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi Revenue Authority impounds 42 kilos of Indian hemp in Mzimba' to a friend
Sports outfit Southern Region Football Association’s new sponsors Nsijjere have announced that the league champions would pocket K7.5 million for...
Mbuzi za custom zikungolephera target ntchito kuba basi mukulimbana ndi zimenezo.
Back pulling,ogolitsa ziwaro ndiye sport free,che mtira mmmxxx where is nacipanti?
Va ziii! Kumupatcha galu wakhoza kulavula.
In fact the poilce know dealers in chilobwe,ndirande and kameza and they just collect tithe
mukatero mukagulitse ndinu ngati mwaoda. …mzanuyo ndiye wachita kugula ….wina ndizamuombera ndimfuti yake yomwe ine
Mra pamozi ndi apolice amene ali ku mra akugwila ntchito yotamandika kwambili koma vuto lilipo ndilokuti pakakhala mapulomoshoni amene amapasidwa ndi anthu okuti ndi ana. amabwana ntchito salimbikila ,komanso amapezeka mwina angochokela kumene ku school kungofikila ku pulomotedwa .pomwe olimbikila ntchito osaganilizilidwa.Bwana IG,Bwana mwapasa aganizileni ana anu makamaka ku MRA timakunyadilani ndipo ntchito tigwila nanu.
Tawasiyani anthu akagulitse inu! Akakudyereni kuti anzanu mmene pavutira pamalawi?
MRA? Not Police? Paja Njoka timapha kumutu osati ku mchila, mumupane anakaoda kuti mukapezako chamba chambili mwanva? Uyuyu ndiosalakwa ayi he is doing what he knows Best, ndiye mwina amatha yachambayo ndiye mumudyetsela banja lake amene akulima alipo? Brute MW Police and MRA, katundu angodutsa wa amwenye osalipila mukulimbana ndi mmalawi mzanu uyu, Stupid.
Why waste your meagre resources on this man when you could have impounded lots of tons at the Matafale Memorial Show in Chileka Blantyre. And this was in full view of the Police. Za double standards basi!!!!!!!!!!!!
aaah akupangiranji zimene a MRA, they should have waited for the product to fetch market and in return they should get their tax………..simple