Email a copy of 'Malawi ruling DPP wins by-polls, add two MPs' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

71 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
KK
KK
9 years ago

DPP ndi machine dala!!

Changoima boy s4
Changoima boy s4
9 years ago

Zamkutu basi DPP ndiye boma len ileni mu 2019 Dpp idzatenga ma seat 173 enawo adzagawana otsalawo.ck woyee,chapananga woyee,changoima woooooooooyeeeeeeeeeeee

Hon Dickens Chipalamandule Ngoma
Hon Dickens Chipalamandule Ngoma
9 years ago

Kumeneko ndiye kubwera booo! DPP WOYEEEEEEE! Prof APM woyeeeee! – CONGRATS!

real life
real life
9 years ago

Amalawi when shall we stop the tribalist bickering. sizitithandizatu zimenezi. timange Malawi with people who can lead our country with passion and deligence.Remember, there will be none outside our Malawi that will come to rule us. Ine zazigawozi zimandinyasa ndi ndikunditopetsa koopsa. Tikumutaya tokhatu malawi. tikuchedwa nazo zimenezo. lets rise above partisan politics and build our nation.

othere countries akutiwerenga kuit kwathu nkukangana. tiyeni tizilimbana ndi ma investors kuti kodi ndi chiani angapangire Amalwi, nanga mpati tili loose kuti dziko lathu liyende bwino osati ati hee achakwera, a msowoya, peter. nzachabechabe zimenezo abaleinu.
tiyeni tikhuzumuke

anonymous
anonymous
9 years ago

ine kimva kukoma basi DPP the party of the people

budadiko
9 years ago

Ine ndine wa chigawo cha pakati. Ndinavotera MCP. Ndimakonda MCP. Congratulations DPP kuti mwaiwina, apa zasonyeza kuti anthu akukondani apa zobera ndikukhulupilira kuti panalibe. Ndimakonda chilungamo tha is why I am congratulating you the DPP koma ndimakonda MCP. Chenjezo kwa inu anzanga nonse a MCP and especially the Centrals. Chakwera wants to sell us to the mortherners. northerners ndi anthu odzikonda, they just want to use MCP through Chakwera za Fedralism. Mulekeni Chakwera adzathandize the northeners koma ife ayi, Chakwera akulamulilidwa ndi mkazi wake nya Kayira wa ku Rumphi ndichifukwa chake anasankha Msowoya kuleka kutenga a Sidiki Mia kapena a… Read more »

mario pei
mario pei
9 years ago
Reply to  budadiko

Chakwera is a hopeless hope for MCP ndipo sandzalamulira Malawi koma palibe chifukwa kukwatira mai Nyakaira she is a well mannered lady with natural looks a good example and good model for all the skin bleached crew

kanchenga
kanchenga
9 years ago
Reply to  budadiko

I am sure you don’t come from the centre and I can understand the pain you are taking to convince the chewas that they are better off with the lomwes. Unfortunately the chewas are neither comfortable with the Nyika nor the lomwes. You are all useless where developing a country is concerned. The tumbukas are good clerks and lomwes make good manual workers and policemen. Oh ooh and good thieves too. Federation is a waist of time Chewas please come back home. You southerners and northerners go home. You mama is lonely. GO HOME GO HOME GO HOME……..

chinyama
chinyama
9 years ago

Mbwenumbwenu, learn to respect your friends. This should not be a platform to insult people.

chinyama
chinyama
9 years ago

You mbwenumbwenu kutukwana anzanu? learn to respect your friends

Kabwiro
9 years ago

Next tifuna referendum ya Quota System kenako federalism tiwone maganizo a Malawi. Nanga si inayamba ndi quota system before the so called federalism?

Nambewe
9 years ago

D phi phi boma ilo

Read previous post:
Zodiak TV to launch ‘family brains showdown’

Zodiak Broadcasting Station (ZBS)  has unleashed another first in Malawi; Family Brains Showdown, an unprecedented thunderbolt television family edutainment masterpiece...

Close