Email a copy of 'Malawi set aside K4bn for maize purchase to avert hunger: Goodall says Admarc to do the buying' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi set aside K4bn for maize purchase to avert hunger: Goodall says Admarc to do the buying' to a friend
It does not rain but pour for President Peter Mutharika who after being described as an “Executive babysitter” by Leader...
Buying maize within the country means the defeceit will still be there.ADMARC USE THE BILLIONS RESIPONSIBLY KOMANSO timalipiro ta antchito anu timamvetsa chisoni
INU PALIBE NZERU APA.I UNDERSTAND KUTI CHIMANGA NCHOCHEPA.THE QUESTION IS MUGULA CHIMANGA CHOCHEPACHOMWECHO NDICHOLINGA CHOTI MUTHANE NDINJALA????????? NOSENSE!!!! ALIMI CHONDE MUSAGULITSE CHIMANGA CHOCHEPA CHOMWE MWAKOLOLA MUNGAZALILIRE KUUTSI. THE GOVERNMENT SHOULD CONSIDER BUYING MAIZE FROM ABROAD NGATI CHINGAPEZEKE SO THAT THE DEFICIT OF ONE MILLION METRICK TONES SHOULD NOT BE THERE.IF GOV DARES TO BUY WITHIN MALAWI I FEEL THE ONE MILLION METRICK TONES DEFICIT WILL REMAIN THEREFORE NJALA IZAVUTA.
timve ziti bwampini ati 10 billion wina ati 4 billion mbava inu eti mxiii kungozolowela kuba agalang’ande
Come to buy maize in Tanzania so as to improve our relationship as well as our economy!
My understanding is that the country will not harvest enough maize for the coming year. Buying directly from the farmers is of course needed. But where will the shortfall come from. The silos? Outside? If the latter, is there funding to import maize, or will we be depending (as ever) on donors.
Twice this article mentions “rooming hunger”. This will seen by foreigners who will raugh their heads off at Marawian Engrish.
Boma likanasiya chimanga chomwe chilipo mudziko muno, nkukagula kunja. ichichi asiyire ma local citizens adzigulitsana. Likanaperekanso zipangizo zotsika mtengo kwa alimi amene ali ndi madimba, nkuwalimbikitsa kuchita ulimi wamthirira, pofuna kuchulukitsa chimangacho popita ku third quarter ya chaka chino.
not rooming but looming mulibe ma editors kodi?
Zazii we want 92 billion and the return of donors full stop
Boma lonyopoletsa anthu bwino kambwiri, komabe chimangacho mugule kunja basi. Ndiye iwe chasika(chakwera) utokote zabwibwi zakozo. kodi kapena mrs cashgate ukumakuuza zochitika kapena munthu wofoira iwe? zako jzu tembo samatsusa mene ukuchitira iwe.