Email a copy of 'Malawi soldiers face allowance cuts in DRC' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi soldiers face allowance cuts in DRC' to a friend
The Volleyball Association of Malawi(VAM) has criticised volleyball committees in the country for allegedly failing to make full use of...
Mukuseweretsazo ndi same kutenga galasi mmanja
Boma lipindulepo apa.why not government benefit all trainningand expenditures?
Guys, just overthrow the government and they should see how important you are. Otherwise, they will finish you off.
Nanu aboma osayamba mwaona anthu ot nkuwabera?MDF if this wil pass show ur work in ths gvt.
Thats not fair but may b its what u have agreed with them do it …..ine ndesindidzakuvotelaniso a president mukangovomeleza zimenezo
Guys, you have the guns and fighting techniques what are you waiting for? Fight the idiots who are cutting your allowances to feed their protruding bellies.
Pliz leave their allowances alone. Ntchito njophana iyi. I hate this no problem guy, idiot.
Masoja a Ku Malawi tulo. Kundoya, kupepera.
Pano mukuphunzitsa a Police za Military, Mwasanduka ma game rangers ku Dzalanyama, kenako muyamba kulondera mmipandamu, kenako tikupangani hayala mma ukwati kulondera ma K50 ofupa.
Ikakhala Ration ndiye munayiwala, ma barracks nyumba kuchepa mpaka kukagona ku rent ma solder.
Pano ka allowance koti mwapangira risk moyowanu akutapanso, kuthandizira mavuto a zachuma ku Malawi. Mwasanduka security company yoti client akalipila mwini company amatenga zonse inu nkukunyotsolerani?
Wake up from Slumber. Osapepera, Apolisi akuposani inu.
Ma Soldier a ku Malawi…..kundoya kwambiri.
ACHITA BWINO KUKUDULANI MUKUKASAMALA MAIKO A ENI KULEPHERA KUSAMALIRA NKHALANGO ZANU KUNO MBUZI ZA ASILIKALI
slashing their wage is inevitable, what do they do to deserve all that money anyway?