22,000 tickets 4 such an international match, what a joke, does the stadium sit that capacity? Bullets and Wanderers can fiil the stadium 2 capacity. Tickets wil not all b sold cos pipo r disappointed with the performance of the Team. Sorry 4 the slow sale of tickets. C u Monday on the comments.
Kunene kude
8 years ago
Tikamapanga maintenance nyumba sitimagwesa yonse apa nde a enerst mwanya nayo kuteroko umawona ngati ndi under 12 mene umatenga iwe gabeya kusiya kamwendo, bajo aah munthu ofoila
Hassam jussab
8 years ago
Vip make sure there are chairs to seat
Hassam jussab
8 years ago
If we want to lets put full bullets team and u c the results
DO NOT LOSE AT HOME BOYS. THIS IS UR TIME TO PLAY GENUINE FOOTBALL NOT FLOWERLY BALL { KUSEWERA MPIRA BWINO KOMA OPANDA ZIGOLI} MPIRA NDI ZIGOLI + KUSEWERA BWINO. KOMANSO BOLA NKHUNTHAZI,OSATI M’BUYO.
CZ 1982
8 years ago
Koma coach wathuyu akusewelesa ntchitoo apa sipoyesela timiyendooo, ma results ndi omwe coach amatchuka nawoo iii kaya apa CV yako ikada who will clean it for youuuu
Dont bother,we in LL and MZ sitingawonere nawo tudzi ta mpira wa ana,we know the results Malawi will lose or draw,@ the end of the game mablantyre akhadzulirana ndalama za pagetipo…eishh
za zi
8 years ago
Kukawonera gemu iyi ndi kubesa.
Palibe chikachitikeko kumeneko.
Mwati flames kaya? Akayithiranso moto as usual and it will be the end of coach.
Ndipo Gudulo Gondwe adule ndalama kumeneku. Chingotithera ndalama chi timuchi ngati DPP.
22,000 tickets 4 such an international match, what a joke, does the stadium sit that capacity? Bullets and Wanderers can fiil the stadium 2 capacity. Tickets wil not all b sold cos pipo r disappointed with the performance of the Team. Sorry 4 the slow sale of tickets. C u Monday on the comments.
Tikamapanga maintenance nyumba sitimagwesa yonse apa nde a enerst mwanya nayo kuteroko umawona ngati ndi under 12 mene umatenga iwe gabeya kusiya kamwendo, bajo aah munthu ofoila
Vip make sure there are chairs to seat
If we want to lets put full bullets team and u c the results
Mukawonela nokha….
DO NOT LOSE AT HOME BOYS. THIS IS UR TIME TO PLAY GENUINE FOOTBALL NOT FLOWERLY BALL { KUSEWERA MPIRA BWINO KOMA OPANDA ZIGOLI} MPIRA NDI ZIGOLI + KUSEWERA BWINO. KOMANSO BOLA NKHUNTHAZI,OSATI M’BUYO.
Koma coach wathuyu akusewelesa ntchitoo apa sipoyesela timiyendooo, ma results ndi omwe coach amatchuka nawoo iii kaya apa CV yako ikada who will clean it for youuuu
So everyone will buy in Blantyre? What about those from Lilongwe and Mzuzu?