Email a copy of 'Malawi teacher students convicted for examination fraud' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi teacher students convicted for examination fraud' to a friend
A chief suspect in Malawi's "Cashgate" corruption scandal, who was a high-ranking official and financier of ex-president Joyce Banda's People's...
Old Dull Learners»nivinthu ngati. Shame on you guys
Onsewa ndi a ku North eeeeti?!!!!!!
Koma Ophunzitsa Dera Lakwawo (ODL) Mpakana kulowa ndi 4n Timayeso take tophweka tija? Azanu tidalemba bwinobwino
muhahaha kikiki mr maliseni kma ngakhale ali ma student ,kma they regard them as teachers.nanga anenako kuti student nurse,student police officer bt STUDENT TEACHERS.ndakomoka kaye kuzolowera kubera adabelaso zisankho ndimastudent teachers nanga kupeleka mimba.mhahahahahahahahahaha kotokotokoto kikikiki 35% gud one
Ndiye angakaphunzitse chiyani ananchidwe amenewa kwa ana?
APHUNZITSI MBUZI KWABASI BT U WANT SALARY INCRIMENT 24% IJA IDAKAKHALA BWINO AKUPEPUTSA MAPHUNZURO
You idiot those ar student teachers not qualified ones so wy do yu insult all teachers? It only sho dat u ar foolish,,wat has salary increment to do with s.tchers?foul
mbuzi za aphunzitsi!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Mastudent teachers kubera mayeso? Koma ODL abale sizinthu, mayeso amene aja mpaka kubera, taonani mukutukwanitsa aphunzitsi onse apa zandinyansa…