Email a copy of 'Malawi to buy another presidential jet' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

78 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
jackson mabokngwane
jackson mabokngwane
8 years ago

zikugwilizandia ndi ma wealth declarations anu osinthasintha aja. ayi sanali 8 anali 2 ……………………. tiyeni nazoni!!!!!!!!!!!!!!!

bongolwethu jayiya
8 years ago

alomwe tsopano, yanu ija nthawi yanu!!!!!!!!!!!!!!

Ben
Ben
8 years ago

Bwana Nankhumwa apa nde mwayankhula ngati omayi , Apresident athu ngati akupita kukapempha chithandizo samangopita ayi pamakhala appointment booking ndi zina zotero nde mukati ndege ikugulidwa kuti abwana azifulumila izo nde nzankutu ndege siziyenda ngati minibus zathu za ndilande ayi zili ndi nthawi nde abwanawo ngati ali ndi meeting yokapempha nkucha munthu uma bookhilatu ndende and next airport umaipeza ina straight away according to your bookings ,apa kuti tigule ndege yathu yathu sikuti tikusunga chuma ayi koma kuononga ,ndege ya private sikuti angoti abwanawo meeting mawa then azinyamuka ayi ,pali kulipira airspace , pilot wathuyo sikuti zingolipidwa ndege ikayenda ayi… Read more »

Dum
Dum
8 years ago

Wankazi uja anabwera chifukwa cha wamuna uja. Palibe wabwino apa.

fomboni al hilal
fomboni al hilal
8 years ago

Aneba akalemela ndikugula galimoto iwe usawatengele. Iwe ndikusawuka kwako ingogula njinga basi.

elton ndojime mapira
elton ndojime mapira
8 years ago

Ijayi anagulitsira dyera.igudwe basiiiiiiiii!!!peter ndimakina guyz

Keen Observer
8 years ago

It was a grave mistake to sell the other Jet ndale zachizimayi anthu ena akunyoza sanakwelepo ndi ndege yomwe. Sadziwa kuti pali mayiko ena a mu Africa momwe muno to fly there you must go to Europe first?????? Ndegeyo zikhala ya munthu ndi ya Boma. Kamuzu anamanga zinyumba pano akugonamo ndani?? So buy it, it will be government property who ever comes after Peter will use it as well.

issah
issah
8 years ago

Not like that ife tukufuna muthu otukula ziko aziphanga misewu ndi kusegula macampony kuti athu tisama thawe kupita zikho lawene

Rev.hesaw
8 years ago

Amalawi bwanji timatsalira mbuyo nthawi zonse?dziko mpaka kukhala opanda ndege ndiimodzi yomwe? olo kusaukako ndiye taonjezatu.

Jabex
Jabex
8 years ago

Ndenge igulidwe basi ife sitiyimva imeneyo. Kodinso ulipo mtundu wina woti ungayendetse dziko lino kuposa ife???????????????????????? Kaya ndikukayika!!!!!!!!!!!!!!!!!!

Read previous post:
Mjura weds sweetheart Tiyamike: Malawi celebrity wedding

Malawi’s Airtel Trace Music star winner Sam Mjura Mkandawire on Saturday married his long time sweetheart Tiyamike Chakhaza at Area...

Close