Email a copy of 'Malawi to get donor budget support of K40bn- Finance Minister' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi to get donor budget support of K40bn- Finance Minister' to a friend
The Blantyre City Council (BCC) and the Malawi Police Service (MPS) have warned people against buying and encroaching prohibited land,...
Comment
Kuyankhula kwambiri pamene ena akumvetsera sikuti nkuchenjera ai phunzirani ulemu
palibe wodziwa zonse pabzikoli
Give credit wherh it is due.
Apapa mukudandaula ndi Mavuto azachuma koma tikuva mwagula ndege kuti muzinjoyera koma amalawi suzatheka ngati mwatopa siyani ndale azungu naonso atopa nsano kuthandiza amalawi. Gulitsani dzikoli kwa azungu mwina tione kusintha
Gulitsani mnyanga ya Njobvu mutigulire Chimanga mchakachi
Comment BRAVO GOODALL I KNOW YU INTERMS OF ECONOMY
Koma abale dziko ili! Kodi boma silikufuna kufufuza 90 billion cash gate chifukwa chachani? Ndalama zinaperekedwa kale. We should forget and close cash gate chapter. Mzimayi uja sanaidoje. Bekatire inayamba kufufuza pompopompo. kodi mukufufuta umboni kapena? Madonars
akufana cash gate yonse ifufuzidwe. Anthu one Ababa ndalama kuyambira 2005 amangidwe basi. Osamango sambira mmanja ena zanunso zibwere poyera. Ngati simunabe Ife tizakondwera.
Ndipodi agaluwa andikwana ine aaaaaaa
Western donors are capitalist, if you think you will develop by recieving change from them forget. This is money they buy stupid governments for favours. You see Surestream because.its from UK, you are bowing to anything it does in Malawi. Malawi politicians have slave mentality.
Bravo, bravo Peter, Gudal & Chilima!!!
Once a slave driver always so, after using Africans to build their cities and work under peanut pays and unbearable conditions this is what we get I thought it is payback time. Malawi must sweat and create innovative and dynamic ways of providing for her sons and daughters AZUNGU anakwiya.
are we still in need of donors? Where is our tough talk of “We dont need donors?” I see many reversal,why? Were just campaign gimmicks to cheat voters?