Email a copy of 'Malawi to sell controlling stakes in Indebank, MSB' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi to sell controlling stakes in Indebank, MSB' to a friend
Barely after four days after the Southern Region Football League (SRFL) secured sponsorship from sportswear suppliers Nsenjere for their league,...
LATE ON YOU , YOU WILL SALE LAKE MALAWI. LAKE MALOMBE, LAKE CHIRWA, LAKE CHIUTA, LAKE KAZUNI,THERE AFTER LAGONS AND RIVERS.
SORRY MALAWI.
Mugulitseso Ma galimoto apa convoy yanu bwana
FOR THE SAKE OF TRANSPARENCY PLS PUBLISH LIST OF BAD DEBTS AND RESPECTIVE AMOUNTS AND REASONS WHY THEY ARE BAD FOR MALAWIANS TO HAVE CLEAR PICTURE.A STRUGLING BANK IS USUALLY MANAGED BY QUESTIONABLE MANAGERS.LHM
Jimmy Lipunga at it again….now banks after havoking the transport sector.where is the money bwana..zathu zisanukapena sbwana anu a godwall or apm…
Kaya inu. No leadership skills. Tifa ndithu, chaka chake ndi chino. This is just the beginning.
palibe nkhani apa,ngati mukuwafuna ma share wo osamakangogula bwanji?
zitini zopanda kanthu kulongolola.
MULLI yo ngati atawafuna akakhala nazo Ndalama akagula.Makani opanda nawo ntchito amenewa.Boma kuli konse limagulitsa ma SHARE ngati lapanikizika,kapena silikuonamo phindu. palibe zoikapo ndale apppaaa…ine ndi wa MCP, komanso ndidalipo pamene Bakili ankagulitsa osati chifukwa chopanikizika,koma kuti watsala pang’ono kupuma.Ma share omwe tinkawaona ngati athu(aboma) anali ake ankaopa kuti akawasiya boma lingadzamulande mosabvuta…..
Nde mukutipo chiani apppaaaaa!!!
Mungogulitsa nduna zonse za boma zikutionongera ma tax athu.
How many institutions or people are owing MSB? What proportion is owed by each debtor? What will happen about the bad debt?
asapitetu kwa MULLI ma shares onse!
Tumbukas at lands and lilongwe city are selling plots to foreigners in LiLongwe. Government is selling banks. Someone sold children to Mozambique last week. Next lets sale Muthalika and his wife.