Email a copy of 'Malawi train kills 12 cattle, a driver beaten up' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

182 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Ntambalika
Ntambalika
9 years ago

ng’ombezo amaweta ndani?

MELINDA
MELINDA
9 years ago

mwalakwitsa kumenya dalaiva.tangogawanani nthumbwanazo ndikumenya amene amakadyetsa ngo’mbe mu njanji.

kukanakhaka kwathu,tikanati ng’ombe zagunda sitima.ndipo abusa amathawiratu kuopa kuthithimulidwa.kkkkkkkkkkkkkk

William
William
9 years ago

Chimidzimidzi
/umbuli basi

Davis Makhoza
Davis Makhoza
9 years ago

Leave railway alone,its a protected area. Law is clear,i urge government to sensitise pipo around the railway on this

Ntigua
Ntigua
9 years ago

driver anamenyedwa alakwa chan? Mudzimvere chison

Juddaist
Juddaist
9 years ago

This is trash. The law is clear on this one. It does not even spare a human being, what more about a herd of cows. The number of cows killed has no substance. They were found at the wrong place at the wrong time. Simple!

Ng'ombe mu njanji? Inuyo ndi ng'ombezo mmafunamo chani. Kumenya driver? Walakwa chani? Bwanji simumachotsa ng'ombe mu njanji driver ataimba belu mpaka kawiri
Ng'ombe mu njanji? Inuyo ndi ng'ombezo mmafunamo chani. Kumenya driver? Walakwa chani? Bwanji simumachotsa ng'ombe mu njanji driver ataimba belu mpaka kawiri
9 years ago

Ng’ombe mu njanji? Inuyo ndi ng’ombezo mmafunamo chani mu njanji? Kummenya driver? Walakwa chani? Bwanji simumachotsa ng’ombezo driver ataimba belu kokwana kawiri?

jj
jj
9 years ago

nkhani sikuchuluka kwa ngombe apa

Kamkhwezule Kakang'ono
Kamkhwezule Kakang'ono
9 years ago

Pipo yakhwasula Ku Balaka.

Abiti
9 years ago

Wolakwa ndi mwin ng’ombeyo komabe pangofunika kumvesetsana kangachepe kwa eni ng’ombezo! pempho amalawi tiyeni tilemekeze malamulo kulakwa ndikumenya a driver,kodi analakwa kuima?ndakhumudwa!

Read previous post:
Ex-Malawi army officer arrested over gun sale

Police in the capital city Lilongwe have arrested a former Malawi Defence Force soldier for allegedly trying to sell a...

Close