Email a copy of 'Malawi under pressure to pass Marriage Bill' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi under pressure to pass Marriage Bill' to a friend
The British coalition government has a painted a rosy picture on the way its Home Office has been handling visas...
Zopanda mchere
ndibwino kuwaikila zaka zokwatirana komanso kuika lamulo lokakamiza mwana aliyense kupita kusukulu kuti malawi likhale dziko lozindikira ndi lozeka
Kodi mukati 18yrs is not responsible kulowa m.banja mukufuna mutanthauze chiyani?
18 yrs. Ndizaka zoyenera kulowa m’banja, coz mmene moyo uno uliri 22yrs ndipatali mukungofuna podyera. Ife eni ake achinyamata tikuona kuti 18 yrs ikukwanira
Yavuta donor money. Munadya koma utsi sunatuluke. Malawi kupupuluma ndi malamulo? Lamulo loyambilira apa ndi compulsory education.
Are you trying to tell me that somebody should be free to get married if they are 8 years old simply because its their right ? People should get married when they are matured enough biologically , psychologically and even economically. Sorry to say this , but early marriages which this bill is trying to discourage are a major cause of abject poverty and high levels of dependence in our society. Unless you want Malawi to stay poor for the next 1000 years then their is some merit in your reasoning guys!
Ndipo balibe chinthu chonyasa ngati kumupangila mwina nthawi yoti adzakwatiwe,anthu amatha nsinkhu mosiyanasiya,izi zichitisa kuti uhule upite patsogolo ngati njira imozi yothesera zilakolako kwa omwe atha msinkhu.
Muaphwanyira ufulu a Chawa ndi Mulhako. Mitundu yiwiriyi ndiyokonda ayichukucha kwabasi. They believe in quantity and not quality. Mxiii!!!
The fact that you want to date limit adge for marriage is a significant of rights violation because its not the choice I the individual. Late the choose when to get married
Ufulu kumaulemekeze mbali zonse. Mukuwaphanyira ufulu kuwapangira zaka. Asiyeni ngati Ayawo ndi Alomwe, alibe kuwona zaka, koma kukwanitsa.