Email a copy of 'Malawi woman arrested for possessing Indian hemp' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawi woman arrested for possessing Indian hemp' to a friend
This year, we have been marking 50 years of Malawi’s independence. Malawi’s history has a strong connection with the UK,...
Why waste time and resources on keeping this woman in custody? Is chamba really that bad?
Kenako timva kuti amupatsa 10 year with hard labor. Koma wa Cashgate akungoyenda pa town mtima uli mmalo.
What kind of security is this one? why not tightening the secury where these plants are grown???????? Mxiiiiiiiiii.
Mutayeni palibe mkhani apa osalimbana ndi nacgate bwanji?
SANAFUNE KUTENGA ZA NAC MUSIYENI
Release the poor woman and don’t charge her at all these are effects of rampant corruption at the Governments top level had it been that Big politicians and government officials managed our resources accordingly we would not be talking of people resorting to selling CHAMBA for their Families survival this is also similar to those cases involving Charcoal sellers ANTHUWATU Ndiumphawi ukuwachititsa zonsezi Ndipo vuto silamunthu ayi koma atsogoleri akatangale ngati Arthur Peter Mutharika amene akuchita promote Corruption Mumati atani Kodi nanga Pilizi akabe kenako timuwotche ana ake Akhale pa Umasiye Muziwanzunza STOP HARRASING THE POOR Timangileni achina Mphwiyo, Lutepo,… Read more »
Anakapanga bwanji mzimayi dollar yashupa pa malawi aah koma mutayeni ka mzimayi kathamange pa town, koma masambawo osagulitsatu inuyo mwatenganu.
Ameneyu sanabe ndalama za boma ayi.Chambatu ndi mpamba kusiyana ndi kuba ndalama za misonkho ya anthu osaukafe.Mutayeni ameneyo Inu apolisi mangani anthu a cashgatewo
Mayi odzilimbikira uyu……..bola pamenepa kusiyana ndi kuchita uhule. Usadandaule mkazi akupatsa fine yochepa ndipo ukangotuluka ukanyamule katundu wochuluka kuti uzabweze makobili ako. Anthu odana ndi chilungamo awa,……, akufuna uzichita kudyetsa katundu kuti upate? Shupit!
Abale, stop victimising people ndi Nkhani ya chamba. ikani lamulo lokomera onse including government on this issue. It is not right for the government to be harvesting Chamba on the roads through A polisi. Tandiuzani, ndi liti lomwe Boma linaotcha or publicly destroy all the tonnes and tonnes of chamba chomwe mwakhala mukumatiuza kuti mwalanda anthu? liti? so where is it all? where is the warehouse? it must be a BIG one! and who is paying rent for it? ndiye chambacho! asiyeni anthuwa or regularise the trade and consumption means.