Email a copy of 'Malawian man arrested for selling ‘dog meat’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

154 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Savely Silavwe
Savely Silavwe
8 years ago

too much mphakana kugulitsa galu ngati nyama? Ameneyo alangidwe kuti anthu amene ali ndi maganizo amenewo atengelepn phunziro

Terms & conditions apply

kkkkk. Balaka again

Idrissah Allan
8 years ago

Masiku omaliza chikondi chizazilala,chimenecho ndi nkuluyu mpaka nyama galu apa ndiye mwaonjeza man,nanu anthu kumangodya zili zonse.

nduna ya kumwera
nduna ya kumwera
8 years ago

Ndiye mumumange?? Sakukumvetsani chisoni ameneyo??? Mumuleke,,anthu amadya amphaka,,agalu,nkhumba..zimasiyana chani??? Vuto ndi anthu ankhwiluwo.akafuna zabwino akagule ku cold storage.,.iya

blessings nkhala
blessings nkhala
8 years ago

life bigginz with eating meat dog

Pedegu
8 years ago

Olo mwala anthu akudya bola kuukazingila bwino

wai
wai
8 years ago

Mmmmmm God help us

Madalitso Gaveni
Madalitso Gaveni
8 years ago

kodi ndi angati adwalapo atadya nyamayo? Musiyeni munthuyo bola anthu adziwa kuti mkuluyo amagulitsa galu

pwefu
pwefu
8 years ago

Breach of peace, when actually it brought peace after kukhuta. Wasowa mlandu apa, mtsyeni basi. Revise our laws to be relevant to certain cases

DOBO
DOBO
8 years ago

Anthu amadya FISI Ndiye mukati GALU,chiweto.Bleach of peace? Apa Ndiye sizikuigwirizana ndi nkhaniyi.Bolani adakati malonda oletsedwa.Komanso chinyengo pa malonda mmalawi muno chafikapo.

Read previous post:
Malawi Police clears Minister on Rumphi arrests: ‘Herbalist made complaint’

Malawi Police Service have justified the arrest of late Tasokwa Msiska's children and cleared Minister of Information, Jappie Mhango of...

Close