Email a copy of 'Malawians making too many babies —Health Minister' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawians making too many babies —Health Minister' to a friend
A couple that stunned residents of Zomba city for selling a seven year old relation to a businessperson in the...
Let us not abuse the special privilege which God gave us,producing babies like that and failing to support them its not right seriously.
koma alomwe nde timatoswana ngati mbira pamodzi ndi azathu achawa komaso atumbuka.
taonani momwe titovutikira m’manyumba mwa anthumu.
kugwira ncthito ngati sukulipidwa,mavuto kumuzi.kkkkkkkkkkkkkk
Anthu osabelekanu ndi choncho kuvuta
Alomwe, Ayawo/Achawa listen: Pitani ku school chonde umbuli wanuwu Malawi is too small for your frequent nyeres. All you do all do nkumangochindana basi. School to you is haram, but a person who has gone through school at least will understand when we say we need to slow down on baby making. Majority of u rely on the few relations or complete strangers to assist you with fees if at all they will go to school. Munthu ndiwe telala koma ana mpaka ten, kusoka mwakathithi munthu wamayi. Maximum number should be two per family. Mukuwathera malo ma northerners kusaka ntchito… Read more »
This is a blessing indeed. Being barren is not good. Ndaziona but now God blessed me and I want more babies. Cheers malawi. Go deeper
Tibelekane basi nanga kutaya mimba sichimo? Tiyeni guys go in egypt ku asia kuli population
dr white olemela wke ndani ukudziwa iwe ali ndi mwana mmodzi
Berekanani a Malawi mumapirimu ndikufuna ndizionamo zisakasa basis chitukuko chakwana enawa alindima billion koma alive ana azathandiza ndiponso Madonna azatengako ena mwinanso Tupac nkuzaombolako angapo
We seriously need to run a serious sensitization campaign about this.Ena akumabeleka ana ambiri thinking that government or relations will help them.People need to take responsibility for their own children.Ngati sungakwanitse, visit Banja la Mtsogolo.
Chinanso-MBC TV and radios have the worst programs that dont help to civilize or educate the masses.Let people find some good entertainment through good and radio TV programs.Even pa radio ma announcer kungokhalira kutamika mowa, weekend, laziness, mababiee.Our poverty will get worse by the day.Moreover those that employ for radios and TV dont look at whether the announcer or presenter has a head to think
Ana abadwe basi. Boma lipitilize kumanga zipatala zazikuluzikulu. Nchito ya kuchipinda ndiyoufunika kwambiri. Ngati Azibusa nawonso amyiwala baibulo, kumalira kuchipinda ngati akumenyedwa, koma kuli kusangalala akumva kokuma kwa mayi busa. Ife ndife ayani ife. Tanyozeka basi.