Email a copy of 'Malawians poke MANEB over MSCE exam results' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Malawians poke MANEB over MSCE exam results' to a friend
Dedza Young Soccer FC have accused traffic police officers from Lilongwe of harassing the team during last week’s trip to...
Onse alopwana akuwaika mma course ngati medicine, social science, medicine, business related etc. Atumbuka onse ku education humanities ku Mzuzu university. Eyetu. 5 years iyi atumbuka ndi blackout basi
Rediculous! The first which they call lies is true. Now they are playing around to pass failures from south and send them to colleges. Maneb is not a bpdy to trust. CAREFUL!!
am so jocund to hear that ,before i was panic and my heart palpitate .when their be realesed send for me at ngara in karonga nyungwe.
Okay, is dat so?
Ndy akatuluka please zayamben kunditumizir ine as the head of all school directors in this country (Malawi)
uneson kusimonga mpaka kut akopweche une yangaimanya nambi acimmasyeto waunami nditu kwende nao wa maneb kwereko atelecedye ma nono g.o
Aaaaaa zosakhala bwino ndi pang’ono pomwe, n’zowona anganamize mtundu wonse wa Malawi chosecho ndizaboza, Akatuluka sasowa ndithu.
Malizitsani kuchongako bola aliyese mudzamupatse ma points a momwe analembera mayeso.Kutathauza kuti osadzapereka ambiri kwa okhoza,ochepa kwa opanda nzeru.
A(Maneb) musamavutike ndikutiuza kuti zoti atuluka ndizonama coz zaboza zimaziwika zokha.
Mukayankha amene walembayo amazimva udolo kuti wakuvutisani.
A(Maneb) musamavutike ndikutiuza kuti zoti atuluka ndizonama coz zaboza zimaziwika zokha.
Mukayankha amene walembayo amazimva udolo kuti wakuvutisani