Email a copy of 'Malawians welcome Bullets in Khartoum' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

53 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Autmatic
9 years ago

zangovuta kugnja neba

Jihad John
Jihad John
9 years ago

kodi anayambitsa zomati ‘wamkaka’ zi ndani? A Malawi kutengeka basi aliyense timwa wamkaka… umphawiwu siwabwinodi! ine zimandinyansa bwanji!

Oikonda Bullets
Oikonda Bullets
9 years ago

Wishing them all the best.

yazula
yazula
9 years ago

Bhunyufu! wakutumayo akuphweteketsa wamva chamba eti,ufune usafune Big Bullets iwinabe basi ngati sukumvetsa udzilume pa mkolokolo pakopo SHUPIT!!!!!! Mxiiiiiiii

Dr. Vxorexalho
Dr. Vxorexalho
9 years ago

zabwino zonse the pples team…

Kika Kanawe
Kika Kanawe
9 years ago

My plea to BB supporters to keep on supporting the team financially through the bank account and SMS Initiative.Let’s put the team in prayers the best is yet to come for the peoples team.The government and the corperate should sponsor the team.

TK
TK
9 years ago

a Malawi mpaka Ku Sudan kkkkkkkk

osman usu justin
osman usu justin
9 years ago

Kumamvetsa aMalawi okhala ku sudan osat masapota abullets kkkkkk

Lackson Mustafa
Lackson Mustafa
9 years ago

Wishing Bullets FC all the best in Sudan.I beg all Bullets FC Supporters to continue sending messages to BB 2015 through. TNM network in order for the team financially supported

Adam christon Masamba
Adam christon Masamba
9 years ago

Ndiri ndichikhulupiliro chonse kuti team yathu yokondedwa ya Big Bullets ichita bwino nditu. Ndamumva wina wake amene ali ndi mtima oipa osaifunila mafuno abwino team yathu, kaya sindikuntha kudziwa kuti mtima wake ndiwotani. E,e si fombon imeneyo ndi Al hilal kungobadwa ndi mtima wausatana basi, osafunira azanu mafuno abwino pamene akuchita bwino tizaonana.

Read previous post:
Malawi new diplomats named: Mphonda to UK, Kamphambe to Germany

President Peter Mutharika has hired new diplomats to head Malawi missions in United Kingdom, Germany, Kuwait and other nations which...

Close