Email a copy of 'Malawi’s got talent in boxing, says Mzuzu promoter Big Joe' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

14 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
JB
JB
8 years ago

aMalawi tinabadwa a sanje mumafuna mukhale inu a promoter mwagwa nayo asiyeni anthu amene Mulungu anawadalitsa atukule malawi

JB
JB
8 years ago

Amalawi akanakhala ndi mzungu apanga promote boxing mukamanena mzungu ndi dolo.koma wakuda mzathu mitima ikufuna kuphulilika.Siyani nkhwizi.Umphawi umene ukutivutha m manyumbamu.More fire Bigjoe.Azafa chonchi ndi mavuto awo

JB
JB
8 years ago

wina mukudana naye anakulandani mkazi

zolozolo
zolozolo
8 years ago

Mbava yotheratu imenei amalawi samalani. Yaswa manyumba osaneneka mu mzuzu mpakana ine ndinasamukamo mu mz coz of him. kundende anabwerako coz of his political involvement but he deserve to be locked up again. boxing nkobisalira

Bwana
Bwana
8 years ago

Iwe Professor James…..ako ma boxer uthandiza liti

Jomba
Jomba
8 years ago

Tisamakhale a kaduka…..tidzayamikira liti kodi?

Professor Peter
Professor Peter
8 years ago

Keep it up Big Joe

Mwanafyale
Mwanafyale
8 years ago

Ife tikusangalala kuno…..musova

JB
JB
8 years ago

Thats why we will never develop

JB
JB
8 years ago

Thats why we will not develop in Malawi. We concentrate on critcising instead of encouraging

Read previous post:
Fashion Malawi exhibitions returns

After a two-year hiatus, the Fashion Malawi Edition (FAME) returns this summer with a week-long of fashion exhibitions. It follows...

Close