Email a copy of 'Man to spend 10 years in Malawi jail for robbery: Police recover stolen good' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Man to spend 10 years in Malawi jail for robbery: Police recover stolen good' to a friend
Malawi new music talent Sam Mjura Mkandawire who impressed the judges in the just ended Airtel Trace Music Stars Africa competition, ...
poor malawians,poor thinking capacity
Iwe kokotowa ndiwe galu nkhumba mbuzi atumbuka atani pa nkhaniyi zopusa basi. Xenophobia kwathu konkuno. Amalawi kuganiza mwautsilu bwanji. Its time we should burry our differences and unite as one. Nkhani zizingokhala zomanyozana basi. Nanga thesani ma intermarriageswa poti a chewa ayawo alomwe akukwatila atumbuka and atumbuka akukwatila achewa ayawo asena angulu. Basi nkhani zizingokhala atumbuka alomwe achewa ayawo basi!! Kodi kuli loti lili ndi mtundu umodzi? Never never on earth.
it always does mesmerize me. kodi anthuwa amakhala opanda zovala? surely they must have had some sort of clothes somewhere. osawaveka bwanji?
Judicially ya paMalawi sidzatheka basi
Ma Cashgate convicts kuwapatsa 3 years after swindling billions
Koma akuba a ku Malawi amandiseketsa. They think a DVD Player, Sub Woofer, Laptop, Phone, TV or a radio is something to die for. Kuganiza mwa chimidzi. And anthu a mma komboni nawonso busy kumagula zimenezi thinking life is all about owning these. Stupid thinking you can do without these. You don’t get anything worth your risk by going breaking peoples houses and snatch these appliances from them. You go about selling them cheaply and you still remain poor. Ndalamazo mumakamweranso kachaso. Next you attempt to come to my house, I will blow the hell out of you with a… Read more »
ZILI KU M’MWERA KKKKKK
Bravo to balaka court the judgement.
Well done Boaz, milandu ya cashgate muweruze ndi inu bwana.
10 years katundu wake ameneyu, aja anapakula ma billion nde 3 years
Nde malawi ndikumdziwa ine ameneyo
Anga ndi maso
Yap vey must be punished