Email a copy of 'Manganya blasts MBC over 'Tikuferanji'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

46 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
john mwaniza
john mwaniza
8 years ago

a MBC simukupanga bwino tisiya kuoneratu ife tv yanuyo mudzingothokoza tikuferanji kuti imapangitsa anthu kuti awonereko tv yanu komanso apopo mwalakwitsa izi zikusonyeza kuti contact yanu ndi tikuferanji munauza kuti akhoza kupanga act pakhani iliyonse nde mwalakwitsa tangoyikani episod Saturday tionere ife pomaliza amene wa ika comment yake kaya akuti levelheaded ndiwe opusa ukuona ngati kuti 25million ndindalama zochepa utakhala iwe ukuona ngati ungalole zimenezi

levelheaded
8 years ago

Koma Manganya mutu wawung’onowo ndi magalasiwo ndi parallel. Ena akuti upititse programme yakoyo Ku ma TV enawa, ma TV ake ati? Othawa signal every 5 minutes’wo? You can talk bad about MBC guys but those so called private are not any near to MBC. Try it Manganya, udziwonera wekha ndi ana ako. On Sumbureta’s issue what you should know is every institution has its own rules and guidelines for every employee to follow and the director general being mandatory employed by the president can’t publicise something that’s directly tarnishing his public reputation. Even you Manganya their must surely be some… Read more »

Mac Millan Banda
Mac Millan Banda
8 years ago

Thats bad 4us coz we only watch mbc on sartuday coz of this episode, ganizan bwino a Mbc tisanasiye kuonera ka tv kanuka

mulinga
mulinga
8 years ago

Muli ntchito…. Board Chair mpaka kuitanidwa kuzamvera Tikuferanji? Ana Ali kuti mpaka Board Chair? Sumbuleta slowly akugwetsa MBC komanso making DPP lose elections in 2019. Ntchito iyoooooo

ellina maonjera
ellina maonjera
8 years ago

imwe apute manganya lero sagona sagona ndi mpweteka!!!!!

Oga
Oga
8 years ago

Try zodiak or times tv pasavute

Viyazi Tembo
Viyazi Tembo
8 years ago

It was Sabbath day either way, don’t fume Mr Usi, mukufana kupanga ndalama mutsiku la sabata?

OBAMA
OBAMA
8 years ago

JB was really a democrat and shall live to be remembered. we could see Peter Muntharika, Chakwera, and all other political leaders on MBC freely castigating Joyce Banda but she never complained. Ndizomwe munkafuna izi ndipo simunati. Since 2014 muone apangapo chani a DPP apart from kugulitsa MSB.

truth
8 years ago

tangoyifunira njira episode yo tipange download basi.Changu pa malo.

Sailota
Sailota
8 years ago

I am very happy with this development. Tinkanena anathera msiiizi! Zayamba kuluma mwini. Simunati mulila mtoooooo!!!!!!

Read previous post:
Uladi presses for Joyce Banda benefits as Malawi ex-president

Leader of People's Party (PP) in Parliament Uladi Mussa has made a frantic plea to government to give former president...

Close