Email a copy of 'MBCtv blacks out Tay Grin’s 6th July performance' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MBCtv blacks out Tay Grin’s 6th July performance' to a friend
The United States of America (USA) has said there is more that needs to be done to ensure public reforms...
The truth is this guy ndi wa matama… good to deflate his big head sometimes… he is far from the best… he is just spoilt
Maybe the football news was more news worthy than Tay Grin as Millions of viewers were eagerly anticipating the match than an old song
Mmmmmmmmmmmmmh! Chifukwa ndi ameneo ndie kuikoka akanakhala gwaladi,chibade ndie olo kukambapo koma p0ti uyu amake amadziwika ndi boma ndie ndi nkhani malawi ndie ameneo!
Palibe nkhani apa. He ddnt do it deliberately..no nsanje. aftr all tinaonera e rest of his perfomance.
mmmmh… dolo ndi dolo baxi or mupange sanje…. taygrin ndi waakulu….
Milanziyo ndamvesa nyimbo inja ndi yakale apeke zina za tsopano two by two yatikwana kwambiri kkkkkkkk tikufuna za sopano
a nyasatimes kungofunaaa kudanitsa anyamatawa apa, Pali nkhani pamenepa?? did Tay Grin complain to you about it?? aaah guys be serious. Nyasatimes, are you always happy when people talk ill about others on your forum?? ndi chiwanda, chani??? What kind of news forum reports negatives only??
Popeza ndi mchewa mchifukwa cjake
HEHEHEHEHEEHHEHEH ANAMUCHITA BWINO. THIS IS GOOD NEWS.
Tipresenter ta ku malawi,iiih!malawi sadzathekadi ndithu.