Email a copy of 'Mchinji Secondary School students damage property, charged by court' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mchinji Secondary School students damage property, charged by court' to a friend
Malawi’s international cooperating partners have called for a "speedy and transparent investigation" into the murder of Anti-Corruption Bureau (ACB) director of...
Akuluakulu Anawa sikuti ndi Openga,ma sukulu ena amaonjeza kumango nyemba kakakaka..muli inu mungave bwanji??mukuchita kudziwa kuti lero tipume Nyemba pokalandira kukaonaso kuti ndi zomwezo…kudya ndalama basi…
45pin alipire koma mukuti 35pin ku xool 15pin ku boma, totaling 2 50pin?
Ana odikira quota awa.They don’t hv any ambitions.They are waiting for their cheap govt to spoon feed them to the University.
Fines paid so fast? Kwacha yathadi!!
ZITSIRU ZICHOTSENI ZIKAPITILIZE KUDYA NYEMBA KUMUDZI KWAWO.
I also did this @ robert laws in 2008 hence i cant blame them, sometymz in these xoolz they r very poor admn & 4 sure this wz not the first tym 4 something lyk this to hapen
But why Malawi? Timadzichedwetsa tokha ndi chitukuko. Anzathu zinthu za 1874 zilipobe koma ife hmmmm. I think this generation deserve perish basi. Talephera kukhala, kusamala chilengedwe talephera.
Ana osavinidwa awa. Kunvetsa chisoni. bwanji kuvuta dziko lanu with meagre resources. Expell them completely kuti azikagula petro ndikuyamba kuba. Senseless kids. These 45 to hell.
Koma abale chizungu chikumalembedwa pa ma comment-wa? Spellings, Grammar and Logic, all below 5%. Khomo la sukulu ngati linasowa chonde lembani mchichewa.
They have to be disciplined accordingly for their misconducts.