Email a copy of 'MCP demands DPP govt to resolve judicially strike' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chithope
9 years ago

Nonse mukunyoza maiuyu Mulungu akukhululukiren poti simukudziwa chomwe mukuchita.Zodziwika mzakuti anthu akumwera tatopa nanu mwaba kokwana so misonkho mukubayi siyathonje kapena tiyi 90% ndiyafodya wakucentral kuno.Fedral ichitike bas kuti muzikaba za thonjezo.

chivwamba
9 years ago

2005 audit ikufunika. Without that Malawians will not rest. You cant hide. Just do it to avoid further embarrassments

Kenneth ngwali
9 years ago

Abale ngati palibe chithandizo zotsatila zake ndizotani?kodi ikanawina mcp mukuona ngati zinthu zikanasitha abale chonde tisavere azimai oduka mituwa ayi atipepeletsatu awa ngakhale bible inakana zoti nkazi alamulire mamuna tsono za a kabwilazi iyi ndiyeno mentally tsopano abale tawatengereni ku zomba mwina alongosoka.john sanagwirepo nchito chuma chomwe alinacho anachipeza bwanji cicilia kadzamila anali air Hostess wa kamuzu osati nkazi wa kamuzu tsono chuma chake anachipeza kuti? Tsono inu akabwila musatitenge ngati kuti ife ndife anthu osaona kapena opanda nzeru tidaphunzira ndipo tikuopa kudzaona zomwe adaona makolo athu ndi ulamuliro oyipa wa mcp lero onani kuduka mitu kwanu muti mufuna federal… Read more »

mwewo woyiba
mwewo woyiba
9 years ago

the mistake muluzi made was giving the judiciary their own fat salary scales as opposed to other civll servants. why should their salaries be different from their fellow civll servants. are they any better than doctors? after all our lawyers turned judges are no better than liars and crooks. all civil servants should operate on one salary scale listening to these selfish people will take us nowhere. muluzi favoured the judges for crooked reasons ie to be favoured in all his cases. muluzi messed up/spoiled things in the civil service please don’t listen to the judiciary support staff. they are… Read more »

Wakukaya.
Wakukaya.
9 years ago

More strikes.Wait just soon Health personnel under CHAM will go on strike.Leave grant arreas for 2013/14 not paid,new salary structure plus arreas not there eeeshi!!!boma lokanika ngati ili sindinaliwonepo.

Old APM
Old APM
9 years ago

Tiyeni naye ameneyu, amaona ngati boma ndi masewera.

Fathara
Fathara
9 years ago

AZIMAYI WOPENGA SOPANO. KODI IWE MAMUNA WAKO NDANI??? TAVOMELEZA KENAKOTU UGWA NDI BP. KOMA AMENEYI ALI NDI MWANA UYU AMABELEKA? Eeeeeeeeh!!!!!! KKKKKKKKKKKKK SICHINGA BELEKE ICHI ZOSATHEKA. CHINANYANYA KUYIPA MOYO. AZIMAYI APASI PA NYANJA AWA SASOWATU NKHOPE. Eeeeeeeeeeeh NDALE UMAZIYESA ZAMASEWELA UVINA NAZO GULE SUNATI. NZIMAYIYITU KUKHALA NGATI KUNKHOPEKO WAVALA CHIGOBA CHA NYAWU TAMUWONENI, TAYAMBA WAVULA KAYE CHILI KU NKHOPECHO KUTI TIWONE NKHOPE YAKO MMMMMMMMM. AKUTI ANDALE APA MALAWI AMENEWO AWAWA??? NDIYE ANTHU AKU SALIMA MUNABESATU Iiiiiiiiiiiiiiiiiiii koma ndichani chimenechi abale??? Zowophya ndithu tiyeni nazoni. Utafikile 2019 uvula chitenje iwe uthamanga misala ndi chamba chako umasutacho.

citizen
citizen
9 years ago

apo pokha tasiyana, Im MCP, but asamvere agalu a judiciary. pepani

Bongololo
Bongololo
9 years ago

Let’s be honest here; donors have nothing to do with our economy, we ourselves have everything to do with what’s wrong with our economy and why we can’t get it together. Now regarding the judical strike, a number of years ago while he was Minister of Education, Mutharika was faced with a similar situation and went into hiding only to emerge when the situation was calm and resolved. His silence on this matter brings back a familiar taste and it’s not a good one for those that went through it. But the difference now is that he is the president… Read more »

Read previous post:
Onesimus drops new single, to be featured in South African movie

What seemed like a never-ending silence by South Africa based Malawian gospel artist Onesimus (real name Armstrong Sopani  Kalua) has...

Close