Email a copy of 'MCP MP Nkhata donates cement bags to Kasungu Market' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP MP Nkhata donates cement bags to Kasungu Market' to a friend
President Peter Mutharika has put a brave face following the International Monetary Fund (IMF) suspending of loans to Malawi for...
Thank you hon Nkhata, Tamvanso kuti ndi team yanu ndi Mayor munapita Ku Shayona, kumeneko ndiye kubwela! Koma mabrick structures akuoneka bwino Kasungu market ikusintha, koma chonde madzi, zimbudzi ndi magetsi zikufunika msanga!
Inu aKandodo khalani pansi Neale zopusa ayi, munadya 1.8 billion ya stadium, munadya ndalama zoti misika imangidwe kawiri, ndiye ife siopusa ayi!!!!!!
Simplicity, u luz nothing thats the type of MP we want. Thanks Nkhata.
Wel done Nkhata,umathandizana pamavuto.Anthu opusa akuona ngati kampeni.Koma nanga inu mukadatani abale anu zitawachitikira.ANkhata 2019 BOMA, MCP BOMA,Chakwera BOMA.
Proper structures are the ones to be constructed not zisakasa za matabwa & cartons to avoid reocurences of these damn fires.
Well done
Cheap politics. Ndale za umphawi ndi umbuli. Sanudi akukatani ku Kasungu kuti akhale Chairman osawasiya eni ake Achewa bwanji M’jomba?????
Afana ofewa
Umathandiza kumene unavoteredwa kumene.MP wa Ku Nsanje anathandiza dera la Kwao nthawi ya ma flood aja!
No need to pose to the camera; palibe nkhani apa.
MPs should be exemplary. A friend in need is the genuine friend.
Zabwino izi.