Email a copy of 'MCP upbeat of Mzuzu councilor by-elections' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP upbeat of Mzuzu councilor by-elections' to a friend
A third year student at University of Malawi’s Chancellor College in the eastern city of Zomba, Paul Macheso thinks Malawi...
DPP EVIL PLANS HIS CANDIDATE IN THE WARD DISHING CASH TO WIN ELECTIONS
Mwayambapo mukaluza muziti mwabeledwa.
Narutah!
Ndipoooo pulezidenti azidzipereka chonchi osanyozera kuti poti campaign ndi ya counsellor ndiye osapita uuuu sibwino iiiiiii mwachita bwino kwambili BWANA wanga. Ndipo amene mukuwapatsa supportwa akukopelaniso anthu ambili komanso it’s through such that you get to endear people. Mwachita bwino BWANA be president of the people. Nthawi youyendera anthu ndi ino, bravo bravo bravo
I would rather support MCP other than supporting people who are robbing the country. At least I can see MCP infrastructure still standing. Tima infrastructures ta a Bakili Muluzi tinatha kale kale. A APM ndi awa mutu wangoima, kusowa chochita.
Anthu omwe anali pa msonkhanowu atavota mawa nde muziti atibera . Simungawone nokha kuti kunalibe anthu? Anthu akulephera kupita ku msonkhano chifukwa akukuopani? Nde muwina bwanji?
Inu a mcp unzingokhalila zomwenzo from 1994 mpaka lelo mukupanga ndale za Kamuzu zomwe zija
A MCP a simple reminder.ngati DPP inawina pangono kumpoto pangono zedi pakati kodi vuto ndi southern region abale majority rules.chisanzo anthu Ku Zimbabwe anthu amati Mugabe sawina panopa koma amaluza.amalawi ziwina kuti majority ya amalawi ilibe access ya internet ifeyo panopa tikhoza kunena izi nndi izi koma nthawi yovota anthu sawonera kwambiri the weekness ya chipani pamalawi vuto ndi regionalism we can’t change it nw.DPP south DPP central MCP north DPP iliko pangono mwina poti panopa pp mutu wake sukuwonekera kwenikweni mwina MCP ndikuzatenga majority koma the fact remain DPP ili ndi majority kumwera ngakhale pamalawi in general we can’t… Read more »
Viva malawi,,,viva mcp,,,,viva DADA CHAKWERA,,,,Tilowaso boma came May 2019
Kodi msewu wa KARONGA chitipa si dpp inu kulota eti ndi mcp.chitsitsi cha dpp ndichoti ili ponseponse ngati inawina akutsutsa nanga pano.mcp frm 1994 imangoti panopa panopa tiwina masewera eti. Muziwina pa central ndi ma 90% omwewo
Munthu wina kungotha nthawi yake kudetsa chipani cha MCP. Ngati umamva mselu ukamva dzina la MCP, uli ndi vuto. Kunja kuno anthu amachikonda chipanichi, BP yako idzakwera ukadzamva zotsatira MCP itapambana. Kwachaaa!