Email a copy of 'MCP welcomes academician Dr Sikanda in its fold' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

41 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
caswell Thom Mbalinga
caswell Thom Mbalinga
8 years ago

maule tonse tajoina

Mkhalakale Songazaudzu
Mkhalakale Songazaudzu
8 years ago

MCP is the only party that will rescue Malawi ku mbava basi. Kungoti a Malawi pepani

Ameneyo
Ameneyo
8 years ago

Tichenjere ndi matchona onse regardless of whether they join MCP, DPP or Chpani cha Pfuko?

Mlauzi
Mlauzi
8 years ago

Defected, not deflected

S. K
S. K
8 years ago

Palibe Chiona ine, munapha anthu ochuluka inu magazi awo anakangamila pa zovala zanu. Mmanja mwanu mwadzaza ndi zinthu zonukha. Mudazunza momvetsa chisoni ma bishop a chikatolika chifukwa chokudzudzulani nkhanza zanu. Mulungu adakuiwalani. Yambani mwalapaaaa! Mwatenga munthu amene wagalukila Mulungu polalika za uthenga wake kuti akhale mtsogoleri wanu. Zoona? Iwalani zodzalamulira dziko lino. Ngakhale mupite kwa ayaya sizitheka. Mulungu adzazutsa ena mwa ang’onowa kuti awete nkhosa zakeeeeeee!

Truck Driver
Truck Driver
8 years ago

Mcp yagwira mseu asafuna akakolope nyanja

Zachisone
Zachisone
8 years ago

A MCP MUNATUMIZA A COLBY BARRACKS M’MUDZI MWANTHU . KUDZAMENYA ALIYENSE CHIFUKWA MUMAFUNA MUTHU M’MODZI. KOMA SIMUNAMUPEZE. NDIMAKUMBUKILA NDILI NDI DZAKA 6. MUNABWELA KUTI MUKABE M’NYUMBA MWA MAKOLO ANGA KOMA CHIFUKWA AMAMETA MALILO A BAMBO ANGA. MUNAGWILILA AZIMAYI, KUBA NDALAMA ZA ATHU A M’MUDZI MWATHU. MCP AGALU INU. MIZIMU SINGALOLE. MUSIYENI PETER SANAKULAKWILENI KATHU. TAWONANI NGO AMBILI NDI MA BWENU MBWENU. KUDZIKONDA ANTHU INU.

chipie
chipie
8 years ago

Alibe chanzeru a dpp. Zakupha leroxo. Munatiyesa2 kudzera mwa Jumbe koma bwa? Inu2 mwagwa nayo basi. Dziphuphani chabe mumalizika 2019 basi.

Joyce Hildah Banda
Joyce Hildah Banda
8 years ago

Is this a Dr really? MCP is the worst hell. When Orton formed it, it had a bright future. Immediately, a nyau guy grabbed it, massacre became order of the day. This is my prophet: vote to became food for ng’ona and remain on margin. You could imagine ng’ombe ndinapereka. why they failed to vote for me? Ine ndikuti MCP ayi

Worry
Worry
8 years ago

My worry is the coincidence of fires with this leader’s movements. I hear he was in KK. Please KK people, step up security at KK market. Do the same there in the North. We don’t want to hear what happened in Kasungu to happen there. It may be mere coincidence but do not take chances! This former man of God may be learning dirty politics in a smarter way. Memories of the Dick Matenjes, David Chiwangas, Twaibu Sangalas, Aaron Gadamas, Orton Chirwas, Mkwapatira Mhangos, Attati Mpakatis, Masauko Chipemberes, The Chisiszas, Kanyama chiumes, Henry Bwanausis etc and so many are still… Read more »

Read previous post:
Economist Kachaje on business lessons from Prophet Bushiri

I am told his title is Major Prophet, or sometimes referred to as Major 1. He has been the talk...

Close