Email a copy of 'MCP youth movement kick off road shows with Msungama ahead re-run ' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP youth movement kick off road shows with Msungama ahead re-run ' to a friend
Songstress Wendy Harawa is bound to make a new impact both on the local and international music arena if the...
I wish I was there
wina amva kuotcha mjekete
Boma lili Ku State house koma anthu mongodzinamiza mudzachangamuka liti? kudzichita ndi chala basis, mbuzi za anthu kkkk
mmmmmmm ndale ndi ndale sizidzasintha or even mwana once join politics nkhani yake ndiyomweo zikupanga nkhalamba zomwez.
andale ose anatembereredwa coz pamaso pamulungu analembetsa kut ndi anthu abodza.No matter kut Msungama ndi mwana but ndale ndi ndale bas.
Tikufuna zimenezo ife tatopa nazo nkhalamba izi
Zikuchita kukongolatu,ma t shirt amenewa ndingawapezeko bwanji koma??? Big up to ULEMU and all MPs who attended this road show and support ULEMU,MCP BOMAAAA!!!!!MOTO KUTI BUUUUUU!!!
Ulemu Msungama, You have my Vote. Iwe ndi Mwana Wa Mulungu. Calvary Family church is behind you. Mulungu wathu SACHEDWA, SAFULUMILA! BRAVO OUR OWN BREED!!!