Email a copy of 'MCP’s Msungama wins elections case against DPP MP: Court orders re-run' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'MCP’s Msungama wins elections case against DPP MP: Court orders re-run' to a friend
President Peter Mutharika has been challenged to provide objective evidence that the Public Finance Management (PFM) System, through which public...
Iwe Nsungama ngakhale by-election itakhala mawa sungawine pa DPP-Namasasu.Udzalira dikira,vuto ukufuna uzaluza ndi mavoti ambiri pamene mpira amatha kutenga world cup ndi chigoli chimodzi. Chende lako wamva kkkkkkkkk
Inu a Clement pali chomutukwanila Msungama pamenepa? big savage indeed
Ulemu ndi deal, komaso fanayi ndiopreza heavy & Mulungu akumumenyera nkhondo! DPP kuba nde kudya kwao!
MCP has a very handsome boy and akuoneka kuti ndi wa Ulemu and it is my hope that he is going to win and get areas of his salaries and benefits from May 20
How to deal with this now… Mwina pano mungomuotcha Msungamayo to make this go for good
Mr msungama,ur de hero
Apulezidenti musafulumire kumapezeka maloamodzi ndi Peter Munthalika , muluzitsa mavoti anthu ayamba kunena kuti MCP ikusapota chipani cha DPP.
Chonde musachite phuma ndikuyamba kumapezeka pamodzi APM . Paja zeru zaukape mulinazo Apulezidenti athu.
Let’s rerun even the presidency!
DPP thinks it can force and impose itself on Malawians you have been setting fires all over to destroy evidence. This judge should be commended for doing the right thing. Corrupt MEC can not hide behind any more fires. just conduct a rerun too bad the same was not done for the May 20th elections. I guess Mbendera got paid hefty loot
i thing the judge is not right the election were fair just let him be the mp why rerun
Zitsilu zikayesa zawina ndiye muwone mmene tizithuzilile ulemu ndi dhilu
Ndikuona kuti judge ivy kamanga walakwitsa coz masiku anapitilira asanacite complaint yake mpaka munthu kumalumbilisidwa.
Ai tiwona ngati a Namasasu atacite apeal kuti zizatha bwanji. Musatiyese ife zitsiru zoti tizikavotanso ai. Mavoti anabotedwa basi sitimangakavote ndi mvula ife ikhala nthawi yamvula.
Ivy kamanga akuwoneka kuti watopa nayo job. Bwanji osangopempha kukapuma?
Ngati ukufuna kutipusitsa ife a MCP sitifuna ai.
Mbuzi ya manu kunsi iwe sukudziwa zimene ukunena. kadye msipu uko