Email a copy of 'Miss Malawi College of Accountancy: Tendai Tambala' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

34 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MacDell
MacDell
9 years ago

Sikuti akati Miss MCA amayang’ana mtsikana okongola kwambiri kuposa onse ai. Kukongola ndikwachibadwidwe simungapikisane chifukwa ndizopanda nzeru kupikisana zinthu zoti sungachitepo kanthu kuti usinthe kapena upambane. It would be unfair for those less endowed with beauty against those with voluptous curvy supple bodies with faces. They also assess confidence and inteliigence. Perhaps our dear sister above outdid her friends in these categories. Okongolawo anuwo analibe nzeru.

aurora
aurora
9 years ago

wina anati asikana aku LLZ ndi nkhwangwa,tikuone iweo bwa and ma sisters ako…kukongongolaa unena iwe ko konzibaya ma jackson or kutikuti,tione chbwez chako bwa mwinaso ndi satana weniweni bolaso aku llz.mwinaso sunagwileko nkazi ngati ameneyu umangohopela,akazi amkukana koz ndi zoba featuriing nkhwangwa ya mnyamata..mubale anu ana okongola wo tizawaone apa,ngati sazakhala nkhwangwa times times/samalani pakamwa,the world is round…

Redeemed
Redeemed
9 years ago

Don’t be deceived by the photo, it might be portraying a complete different picture, also remember that “beauty lies on the eyes of the beholder.”

sello Mvuyane
sello Mvuyane
9 years ago

amene mukuti siokongolanu, kukumana nanu ndinu amuna osaoneka bho, azikazanu nde bolaso ine, ma sisters anu kusasamba mkati zaziii, she is cute

aurora
aurora
9 years ago

mmmmmmmm congrants girl, no one is ugly in the eyes of JAH..jah turns ugly into someone beautiful,apparently you are beautiful..because HE god loves you.dont mind the haters,you are living and scceding because of he haters..pray,AMBUYE MUWAPASE MOYO,ADANI ANGA OSEWO,CHOLINGA CHOTI AZAONE ULEMERERO WANGA,AMBUYE MUWAPASE MOYO.

Peter Mathanyula Wakuba

A nyasatimes a mwano inu. Mwaika dala photo yamkazi onyasa ndicholinga choti timuseke

sayin it like it is
sayin it like it is
9 years ago

hehehehe mwati mr mca kapena miss? if she is the won I don’t wanna see the ones who lost…ku Lilongwe kunazaza nkhwangwa zokhazokha

chimutu
chimutu
9 years ago

wat does it take to be miss?? if beauty is the reason then this one doesn’t deserve to be a legitimate winner. she is actually far below standards. and if the organizers continue showcasing gals of this caliber, I will lament for my country which has pretty beautiful ladies but lack exposure.

Keen Observer
9 years ago

Zingotengani ma Higher Certificate wo, Higher Diploma wo kaya ndi ma Degree osati zopusazi Azimayi abwino bwino muziyenda maliseche pamaso pamuna ndiye chani? Azimayi muzachenjera liti? Always you need to be used like a pawn? Beauty Contest my foot.

Mwanyongo
Mwanyongo
9 years ago

Inu mmene amakongolera atsikana apa MCA ku BT mukundiwuza kuti ku LL ameneyu ndiye wokongoletsetsa? Basi ndizikhala ku BT konkuno.

Read previous post:
Malawi govt bulldozed Macra on $13m ‘spy machine’ upgrade: CSOs demand probe

After Nyasa Times first reported that government has bulldozed Malawi Communications Regulatory Authority (Macra) to authorise payment of US$13, 871.969...

Close