Jinkele (not real name) you are a member of staff at MRA and you have only been there a few months. Your problem is that you hate Kamoto . Your ambitions to be given a top position backfired and you are a bitter person. You cant hide. Your real name is…………….
midrand 2
8 years ago
Momwe JB ankamulemba Mpwiyo nonse munali duu. Akhala kuba onse kenako he was shot nkumatuluka za cash gate munayamba kumunena JB kuti amalemba mbava.
I agree with number 50. Ku MRA kuli mbava bad, nde akamawachotsa mudzimunena Kamoto? Leave him alone ndi zomwe tikufuna ife. Mawa kukapezeka cash gate munenenso kuti amawalekelela? Soldier on Kamoto.
MR PRESIDENT, KAMOTO IS THE TYPE OF BOSS HERE IN MRA THAT WE WANTED. OSAMVERA AKUBA ENA AMENE AKUFUNA KUMUYIPITSA AYI.
Bwana adzitere.
makani
8 years ago
Bodza Kamoto we should not protect mbava enawa ndi azibale ambava zimene mwazichotsazi ndiye osazitengera gwirani ntchito Mr. Akuba achotsedwe ukachotsedwanso ndimwayi wako timayrnera kukumangani anyani inu.
Let Kamoto do his job he is the best solution to the ever underperforming tax collecting body (MRA) we know kuti ambiri akuyankhulawa ndi anthu okanika amene amangofuna mwayi okuba osati kuthandiza dzikoli well done Ralph
kangandiwamba
8 years ago
nditovomereza ndi number 52
vuto kamoto wazunguliliridwa ndi mbava
mbava zake pretends to help him kwinaku akuba zedi
timadabwa ma decision ena a mabwana ku mra
Samala Kamoto
Koma mukamuchotsa dziwani kuti zimene zitatenge udindo wake mbava zokha zokha with personal interests at heart
Shehe
8 years ago
Tiyeni tizinena chilungamo anthu ambiri kuMRA ndi mbava bosses and juniors. Mr President leave Kamoto for 10 years asese mbava zonse. Mbava zili busy kumangoti sizikuenda bwino chani apa. Bwana Kamoto sesani list tikupasani. Phwasulani network anaika ujayu mwachangu osawamvera chisoni iyayi
Mayi Agnes Katsonga iiiiiiiiiiii sindimaiwala m’mene anavinira ati kusangalala atamva kuti Bingu wamwalira.Mpaka kupanga phwando mayi amenewa ati kusangalala.zimaterotu mayi ndikakumbuka m’mene munavinira muja,m’mene munasangaalalira muja ndimamva chisoni poziwa kuti ndi Mayi wa munthu wolemekezeka.
adona kuseli
8 years ago
kumsonkho kumeneko tsopano. Tiyeni nazoni. Wafa-wafa nkhondo ya angoni!!
True Lhomwe
8 years ago
Who said Mr Kamoto is not corrupt? Kamoto just resign before we expose all your deals. Your sex episodes, your night meetings planning to take down government etc
Jinkele (not real name) you are a member of staff at MRA and you have only been there a few months. Your problem is that you hate Kamoto . Your ambitions to be given a top position backfired and you are a bitter person. You cant hide. Your real name is…………….
Momwe JB ankamulemba Mpwiyo nonse munali duu. Akhala kuba onse kenako he was shot nkumatuluka za cash gate munayamba kumunena JB kuti amalemba mbava.
Musiyeni Kamoto akugwila ntchito bwino mwina umbava nkuchepa.
I agree with number 50. Ku MRA kuli mbava bad, nde akamawachotsa mudzimunena Kamoto? Leave him alone ndi zomwe tikufuna ife. Mawa kukapezeka cash gate munenenso kuti amawalekelela? Soldier on Kamoto.
MR PRESIDENT, KAMOTO IS THE TYPE OF BOSS HERE IN MRA THAT WE WANTED. OSAMVERA AKUBA ENA AMENE AKUFUNA KUMUYIPITSA AYI.
Bwana adzitere.
Bodza Kamoto we should not protect mbava enawa ndi azibale ambava zimene mwazichotsazi ndiye osazitengera gwirani ntchito Mr. Akuba achotsedwe ukachotsedwanso ndimwayi wako timayrnera kukumangani anyani inu.
Let Kamoto do his job he is the best solution to the ever underperforming tax collecting body (MRA) we know kuti ambiri akuyankhulawa ndi anthu okanika amene amangofuna mwayi okuba osati kuthandiza dzikoli well done Ralph
nditovomereza ndi number 52
vuto kamoto wazunguliliridwa ndi mbava
mbava zake pretends to help him kwinaku akuba zedi
timadabwa ma decision ena a mabwana ku mra
Samala Kamoto
Koma mukamuchotsa dziwani kuti zimene zitatenge udindo wake mbava zokha zokha with personal interests at heart
Tiyeni tizinena chilungamo anthu ambiri kuMRA ndi mbava bosses and juniors. Mr President leave Kamoto for 10 years asese mbava zonse. Mbava zili busy kumangoti sizikuenda bwino chani apa. Bwana Kamoto sesani list tikupasani. Phwasulani network anaika ujayu mwachangu osawamvera chisoni iyayi
Ameneyu komoto ulendo omangamanga mra akuyesa yamake june akhamla alikunyumba akukanda mimba yakazi ake inunso kamoto kumanyenga akazi aeni kuti muwakweza kuyela kokukhalako kaya usolva
Usove ndiwe sasamba,ndiye uli bwinotu mpaka kunyengeledwa mkazi uzidabwe pamenepo.Sesa Kamoto Sesa mbava Zonse out.Agnes Katsonga Mayi anavina kwambiri ati Kutsangalala atamva kuti Bingu wamwalirayu aaaaaaa zimandiwa ndikakumbukira