Email a copy of 'Moyale, Eagles register wins as Bullets meet KB obstacle' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

7 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Munthu wa Mulungu
Munthu wa Mulungu
9 years ago

Ku Dedza Stadium ma Banker analiko? za chamba eti. Muzingopanga zanu, osamalimbana ndi ma game a anzanu. kodi inu a bb league munatenga liti? nanga mukudandaula chiani apa? Makape!

Ndaonera momwemo
9 years ago

Ma bankers mwachita bwino kuti maulefe tizagagade tokha a moyalewo.Ndipamene muzaziwe kuti Maule ndi chiteam cha nyatwa.

mr soccer
9 years ago

BB YALUZA KODI UYU MUNTHU WABWERA KUDZADYA MILLION ANALIKUTU M’MESA AMATINAMIZA KUTI AKUZASULA MA SITILAYIKA NDIYE NANGA SAKUCHINYA BWANJI?…..PALI GAMETU APA MILLION IGOPITA IYI……………..

CHAKUCHANYA
9 years ago

Bankers kaya inakonza kaya sinakonze zanu izo,kodi bankers imaselera Bullets kapena kuti Bankers ndi prayer wa Bullets,mukhaula zanu izo,Ife ma Bankers palibe choluza apa kkkkkkkkkkkkkkkkk,eish Moyale,anthu kulankhula too much.

Uchindami
Uchindami
9 years ago

Kugonja kwa dzulo kwa BB ndi chikumbutso choti ligi yachaka chino sidathe ndipo mudikire kaye. Malankhulidwe anu inu ochemelera mutagonjetsa Blue Eagles simakhla ngati kuti ligi mwatenga kale. Kulankhula kwa ku mpira wamiyendo sikufunika kukhala ngati anthu omenya nkhonya! Ndiye ndi zimenezi mwaziona dzuloli (26/10/2014).

DR DRE
DR DRE
9 years ago

ma bankers achita mokonza zinthuzi, asatipusitse ife si ana

jumujum
jumujum
9 years ago

BB moto muyale ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii

Read previous post:
Avoid ‘Zidyamakanda’, First Lady advises students

Malawi's First Lady Gertrude Mutharika has commended the Roman Catholic for their quest to offer quality and holistic girl education...

Close