Email a copy of 'Mozambique deport 34 Malawians en-route to South Africa' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mozambique deport 34 Malawians en-route to South Africa' to a friend
Minister of Gender, Children, Disability and Social Welfare Patricia Kaliati has received the Outstanding African Woman Leadership Award at the...
That’s true iwo amafuna dollar ambiri amadutsa opanda passport nawonso apolice aku malawi ku mawasunganso anthuwo chifukwa chani asiyeni azagwire ntchito njala yakula pa mw
Ngongoliwa& Sapitwa, why do you continue advertising your ignorance with that high proportion?
Mozambique turning away malawians,how about the ethiopians,chinese and burundians amadzela kuti? Inde analibe dollar to bribe the mozambicans…..osati trafficking..willungly on an open truck,u must be joking !!
Peter Santa Muthalika on drive seat
Is it human trafficking or the people are going there willingly???????? And on what grounds did the Mozambiquecan Authorities deport the people who were just in transit???????? Didn’t they have proper legal documentation??????? From what I have seen one passenger had a passport??????? The matter of the fact is that they were looking for bribes which they didn’t get. If it were women & kids I could have understood but who can traffick Mphongo?????? Mphongo zimakasaka ntchito.
Passed Dedza border post? Really? Anakufumbatitsani eti or u dont know why you are there? Bwana Chilima, kodi reform yafikako ku ma border post kapena yangothera malo “ogulira” passports?
They have been doing this for a long time. They mostly travel without passports these Mangochi people. They pay bribes right through all the way. Something might have gone wrong where they were arrested or they didn’t pay enough bribe.
mukamati ku malawi kuli zochita ndiye kulankhula mopusa komanso mopanda mzeru tangoganizani panopa kwacha yagwanso 1dollar-654mk ndiye salary ya munthu ili pa mk14,000 lent pomwepo adye pompo wina ndi lover umoyo ulipo! Mmwene ku south africa mu shop amalipira mk35,000 per fort nyt ku malawi ndi mmwenye ndani angalipire chomcho? Muzilankhula ndi kumaganiza ngat inu mukudya mzanu wagona ndi njala
Bwana Masauko Medi……Mwaona anzanu ku Mozambique? I mean how does these trucks pass through our border posts especially Biriwiri and Mwanza when your staff is there?
Inu Malawi wake uti mukutiuza kuti tidzilimayo aaaaaaaaah ine zikakhala ng’ombe nkukolopa nkakolopa akandipatsa 80,000 kwacha yo zanga ziiiiiii kumalawi angandipatse ndalama imeneyo ndani ntchito yokolopayo .