Email a copy of 'Mphwiyo family yet to be charged -ACB' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Wanex banda
Wanex banda
9 years ago

ACB and judges get thd points here raised by patriotic Malawians,MANYUMBAWO ALANDIDWE APO BII FIREGATE ISAWAPITILIRE AMENEWA

S Allie
S Allie
9 years ago

Let’s wait and see for the court to do the job if not malawian will remain be poor forever

OBAMA
OBAMA
9 years ago

Even mu area 47 kuona nyumba mwini wake ndi driver wa boma ku ministry yinayake koma ali ndi nyumba mu area 10 and 47. Ndalama anazitenga kuti amenewa. Cashgate basi with this beauracratic system of government we have causes people to steal money in the government. Amene akukana zotseka account number 1 ndi amene akufuna kuti aziba ndalama za boma and one of them is Atupele Muluzi. Pa debate paja ankakana za maganizo otseka account number 1.

mr man
mr man
9 years ago

yes mrs senzani ali ndi nyumba pa bunda ,kuiona nyumbayo its close to 1 billion kodi ndalamazo azitenga kuti .iwe mphwiyo umati ndiwe odalitsika mchifukwa uli ndi ndalama zambiri tikulanda nyumbayo, mabillion ambiri amenewo ,inu a ac b mukalephela ndikhalapo ndine kuti ndithane nazo

ezy u. k nbimenya nkhondo

chris Nyirenda
chris Nyirenda
9 years ago

INU ACB NANGA TINAWELENGA KUTI PETER D MLAUZI ANACHITA CASH CHEQUE CHA TWENTY MILLION KWACHA NKHANIYI TINAYIWELENGA PA JANIARY 5 CHAKA CHINO KOMA MPAKA LELO AKUTI NDALAMAZO ANAGAWANA NDI AMENE ANALI REGISTRAR WA HIGH COURT MLAUZI NDI DEPUTY SHERIFF OFF MALAWI WOLANDA KATUNDU WA ANTHU OSALIPILA NGONGOLE ACB WELL DONE FEAR NOBODY

lehlonolo majoro
lehlonolo majoro
9 years ago

you stupid fools rush to arrest people without knowing what they did wrong???? acb my foot, mbaza zeni zeni!!!!!!!!!!!!!

chikwangwani
9 years ago

ali tiye nazo mkaziwanga ndalama za a malawizi. nde muzawagamulenso 3 years tiyamba kuotcha nyumba za ma judgetu tikatopa nanu

Venezuela
Venezuela
9 years ago

Fufuzani makamaka ma civil servants omwe amanga nyumba zowopsyeza, amazitenga kuti ndalama like theresa senzanis mansion pa bunda. Zilandidwe zimenezi kapena apo bii kukoleza moto basi tiluze tonse. Naye mphwiyo that house, anamangila ndalama zake ziti?

mthako wa alhomwe
mthako wa alhomwe
9 years ago

kenaka muwalipire ndalama chonsecho mukuchedwesera dala.

Read previous post:
Kamuzu Banda benefits claim headlines Malawi paper

A benefits claim by the family of founding president Hastings Kamuzu Banda to government hit the headlines on Tuesday. Malawi...

Close