Email a copy of 'Mr Muscle and Miss Bikini set to lighten up Easter in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mr Muscle and Miss Bikini set to lighten up Easter in Malawi' to a friend
About 20 cars including luxury vehicles have been impounded and dozens of people arrested on various offences. The crackdown targeted...
IZINSO NDIYE ZA U HOMO. ZOWONA
Comment God will punish you I tell you. Musankhe date lina not during Easter tum
Dziko likupita kuti abale sitikulola satana atilamulire
alomwe si anthu koma ndi zilengwalengwa. Thats why chi president chopopotoka kamwa ngati chapsya ndi dzungu lamoto. Chikungopanga zake zachamba basi. Zonse izi nawo aBakili kukatenga chakufa chija chi Bingu kuchipasa undido. Ifetu mumbiri ya malawi mulibe anamunthalika. Alomwe mahule inu mukunyozesa dzina la malawi.
mulungu si munthu woseweretsa
Mwayenjeza sankhani tsiku lina kapena labour day osati Easter. Mukuputa matemberero kuganiza koperewera ganiza
Zasatanic muyaluka mwayamba kutenga zakumdima kuzibweretsa poyera.Imeneyo ndi ncthito yolembedwa ndisatana.kenako mupanga mpikisano wodya nyama ya anthu chaka chake ndi chino muyaluka.(Hebrews 4:13 )
sibwino choncho..
p
n shidaaa!!
Chisangalalo choti Yesu wauka ndizomwe mukukachita ndizosiyana abale tisasewelese dzina la Mulungu