Email a copy of 'Mulanje woman burns son’s hands over chicken piece, ‘Chinyomphilo’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mulanje woman burns son’s hands over chicken piece, ‘Chinyomphilo’' to a friend
Third accused person in the conspiracy to commit murder of former budget director Paul Mphwiyo, Ralph Kasambara has asked for...
Kuotcha mwana chifukwa cha thako la nyoli zoona kuvuka 9 moths ndi tsiku la labour lija. Pepeani mayi mwadzimangitsa nokha
Kuipa mtima kumeneko amangidwe basi
izi sizinthu koma ndi ufiti umenewu,osewa amauluka ndithu.
mayi ameneyo akhale mundende zaka 10 mai oyipa ameneyo kwambili
winawu si umunthu ndi chiwanda cheni cheni zikufunika mapemphero chifukwa ndikupha komwe uku.mina si wako mwanayu mmayi iwe satana.
Bamboyo mwanayu siwake, apa anthuwa obviously chalichi ndiyochepa
Mayi woyipa ameneyu alangidwe. Mwana umati asadye ali ndi njala? Iwe kumundako ndi mwamunakoyo simunadye the whole day?
Fotseki
mai kusoweka umunthu ndi umwini uyo
Kachinyophironso nkachani kootchera mwana
hahahah very sympathetic I hope we need to ask God’S Guidance evry day tikadzuka….,koma na izi nde zivuta kumvetsa hahaha pepani anthu aku Mulanje tho my woman z oxo frm Mulanje koma nde apa zanyanya.