Email a copy of 'Mulhako hail Ngolongoliwa promotion to Senior TA' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mulhako hail Ngolongoliwa promotion to Senior TA' to a friend
Two children have died in Dedza after eating poisonous cassava as their parents were away searching for food, the first...
Cmment No.3, U are Worthless, Foolish, Good For Nothing! How Can U Vomit like that to the Head Of State & the Lomwes? You Wanted the President to make plans For Your Family on how to get food? Wauponda Wamva! Alomwe Tipitiliza Kulamula Malawi mpaka Yesu Kubwera, Muuzane Zimenezi Ok!
Tikamati ndinu angulu mumanyanyala
zomvetsa chisoni moti Angongongowa mmene mwawasankhilawmu malawi ilemera koposa moti kumalawi sikuzapezekaso mavuto. tiyeni nazo its just a matter of time
My Malawi my country…tribalism at its best from a village headman to a Traditional Authority and now to Senior Traditional Authority…some you will be crowned Paramount Ngogoliwa anyway congratulations.
NKHANI NDI CHIMANGA
CHIPEDZEKA CHIMANGA
KUMENEKO ,,,??
TATOTOPA NAWO MAPEYALA !!.
a mfumu akulongedwa kumene. ufumu umakoma ndi anthu.
Ife tikufuna mfumu yokoda anthu ake komanso chitukuko.
Mwateromo pitani mukawaphunzitse anthu kugwira ntchito molimbika kuti apeze chakudya. tisazamve kuti anthu uku akufa ndi njala namwali watsopano aliko ngolingoliwa wamkulu
kulankhula kwanu pamsonkhano kuja kufanane ndi ntchito zanu kuti anthu apulumuke.
asakhale akudalira za ulele mpaka kale kale
The famous Anguru r fading out completely and have been replaced by the Mulhakhos which is a small tribe, only that the Mutharikas r from this tribe. We wish u u all the best as u busk in ur newfound glory!
Mr. President Sir, how do you make plans for stupid tribal dances when your very own people are suffering and dieing of hunger. In this elevation ceremony you will see that there will be enough food for the rich doing their stupid tribal dances!! Burn in hell Peter Mutharika you don’t deserve any respect from us civilians and we do not recognise you as a president of this country. We are having enough economic problems because of you we are suffering, our fellow brothers and sisters are dying because of you and you would like to celebrate your stupid tribal… Read more »
kodi akhale mere mfumu ndani poti aliyense akumukweza kupita pa U TA . abale its not about the position that makes one serve better. its about hard work honesty.
ine zama ufumu omakweza koz of ndale bwanji zithe. tengeraniko ku mzimba. once born TA basi zimayenda choncho
za ZIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIIII