Email a copy of 'Mutharika meets Malawi religious leaders: ‘Asks for special prayers’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Mutharika meets Malawi religious leaders: ‘Asks for special prayers’' to a friend
Minister of Health, Dr Jean Kalilani has said government with the help of UN agencies will prioritise the campaign to...
Bingunso zinayamba chonchi.wa mwayi ndi mayi wa zingwe za mbuzi uja,chifukwa Chauta anamuonetseratu kuti sangalamulire Malawi.nde kumasamala zisanafike pa kadya kalista (cadiac arrest)pali chiphunzitso chachikulu kwambiri pamenepa.tiyeni nazoni. ali ndi khutu amve ndithu.
Akufuna kupempherela mvula or kudwala misala?koma inu palidi msogoleli apa bolatu JB.
Prayers for what? Mumangomtukwananso chauta INU. Kodi tinatonso ntikofiya kapena zisa za njiwa? Kuseli kwa phada kuli phwandodi.
The president have also of time to waste.
Until now the so called professor doesn’t know meetings are just a waste of time.Kenako timva meeting ndi ogulitsa nkhumba,then oweta abakha…..akammanja….oitanira ma minibus…..ovina dusha……omenya madulira polowa mtauni……a zaufiti……list endless.A Malawi tili mmavuto.Bola nthawi ya John Chilembwe.Mayoooo!
Ngati Mtola khani anaulula za ma envolop kuli bwanji Mbusa kapena Pastor mukhala chete? Nanga womvera Mulungu pamenepa akhala ndani?
Kodi nanga aja a PP Livingstonia Quota System Church analipo, Ine sindinawawone , kapena sanabwere chifukwa anaitana si joyce Banda, ayi dikirani Joyce azabwereranso pampando, muzasangalalanso nayo Cashgate
Kusowa zochita President. Very very clueless. Get a broom and go and sweep some dirty street we have plenty of them.
Alembi ndi Afalisi pose for a photo kkkkkkk moto kwa iwo opondeleza
No 5: Paja Judge Nyirenda amacokera ku Mulanje? Kodi mudzi wanj Bwana?
Ndiye ndinu opusa zedi