Email a copy of 'Mutharika must stop shifting blame - MCP' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

43 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
MaKopa
MaKopa
8 years ago

Mabvuto amabwera anthu akabera chisankho, vuto lake ndiloti APM anabera no on one love or trust this man

Mlomwe
Mlomwe
8 years ago

Bamusi ndi dzina lake la chilomwe si munthu koma thonje lama ARVS.Iye mwadzeru zake sangawone mene prezident akuonongera ndalama?kapena wadya BANS?MUTU WAKO BAMUSI .DPP pa ulendo basi Antcheya adanena kale kuti mukangomva mbuli zikuti ndayiwala mudziwe ndi paulendo basi.Bamusi wayiwala

henry maseko
8 years ago

dpp paulendo basi 2019

defender
8 years ago

overpressing muthalika wil only compress him,reserve mo energy,work hard to deliver his promises & promis malawian even more come 2019. which country has ever booted out of power a rulling party that had delivered its promises/ manifesto.kkk Bingu had a landslide 2009 same scenarial, MCP work up!

defender
8 years ago

ya! mwina mkovutadi to weaken a ruling patty, koma MCP’ strategy of attacking everything, including small issues can not win new members & even maintaining old ones can b difficunt.golden advice losing 2019 could mean end of MCP

nkhakamila
nkhakamila
8 years ago

eeeish MCP you arguments are baseless…wish all the best muzatenge boma 2019 tione ngati simuzamapita ku UN Summit.palibetu nkhani apa…ine sindikuona chimene anthu akung’ambira kukamwa..politicians you have similar interests…ndi business yanu iyi musatipeperesepo apa.MCP=DPP=PP=UDF.MCP Just wait nthawi yanu izafika nanuso mudzadye ndalama…mzosiyirana izi and ife tinazolowera.dont fool us kuti ndalama zopitila ku UN Zikanatithandiza amalawife.if you failed to follow up the money that we got from the jet sale then the UN expenses are just peanuts for us to be discussing.

apao
apao
8 years ago

Mr bamusi.can’t you
see kuti bi deffending this person wotchedwA petulo ur contributing kuti akhale akuchita za uchiselekwete? Instead of looking at mavuto omwe atolankhani akufutsawo. Ur dealing ndi complainer pali nzeru papenepa. JB. Adayesesatu ndipo pp idachita kumbali ya amalawi.koma dyera latibweresera zimenezi

sayi uphak
8 years ago

Uko kunali kulira kwa akulu a dambwe O Chakwera. Pa nthawi ino tipereka mpata kwa mkulu wa amayi a Chisamba a Jese Kabwera Kapasula nawonso atiyankhule malonje awo. Tsano kumapetoku tikudzutsa mwini nkhani chilombo chachikulu Kasiya Maliro alowe mbwalomu, omayi ochisamba onse akhale oli kuyimba manja ndi nthungululu

Hd
Hd
8 years ago

Ngati ufuna kujoina gulu la anthu olephera join mcp

phiri Gabriel
8 years ago

This matter is very simple. The combined list should be made public and the expenses of Govt on the trip publicised. This should be it.

Read previous post:
Mutharika commit to secure funds for Blantyre Water Board

President Peter Mutharika on Tuesday paid a surprise visit to the Blantyre Water Board (BWB) to appreciate challenges hampering the...

Close