Email a copy of 'Mutharika spokesman says Malawi President 'will not resign' despite calls from CSOs' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

105 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
paul mwale
paul mwale
8 years ago

Mutharika must finish his term.

vumbwe
8 years ago

Atumbuka kodi mudzalamulako liti dziko la Malawi? Kwanu ndikuphathikila zipani za anzanu basi AFORD idakunyerani. Noise yonse imene mumapanga imakupindulirani chiani? Pangani chanuchanu chipani osaphathikila kwa anthu a pa central ndi south tione kuti ngakhale nonse mutavoterana atumbuka nokha nokha ngati mungawine. Kwanu ndikukhuwakhuwa komweku basi palibe wakumwera kapena wapakati angathandizire kuvotera mtumbuka koma atumbukanu mumathandizira ma southerners ndi apakati kutiwinitsa basi. Mumayesetsa kuchita mitala kuti muswane, ayi ndithu, mukuchepela kaba. Kaya ndife osaphunzira, koma timakulamuliranibe. Mapulezident are from south and centre , not dead north.

JAPHET KAIRA
JAPHET KAIRA
8 years ago

All the presidents we hav had in malawi are good but only the bad pple are the subodnates sarounding the president.The bad pple like H Mussa,G Chaponda,kaliat etc these are the ones who makes president go astray.who ever will come will not b safe at all,lets just call the whites to rule over us again,we r going to die plz!

H Kamdidi
H Kamdidi
8 years ago

Ofcourse he cannot resign otherwise azikadya chani?

Aubrey Norman
Aubrey Norman
8 years ago

Amabungwe muzitenge bwino mungamanene kuti president achepetse kuyenda yenda?mwati akuwononga ndalama za Boma?kodi nanga otsutsa omwe akuyenda yendawa ndalama zawo amazitenga kuti?mukutiwuza kuti otsutsa ndiwomwe alindi ndalama zocholuka zochititsira misonkhano kusiyana ndi DPP?Mukamayankhula muziganiza kaye zomwe mukuyankhulazo popewa kudzetsa mpongwepungwe.Njala sinabwere chifukwa cha Peter koma chifuniro cha mwini zolengedwa.

mtumbuka selfish dog
mtumbuka selfish dog
8 years ago

Atumbuka amzanga matako anu

Jose'
Jose'
8 years ago

Nsanje si umuna. Mwamva a useless mtambo?

mwachaje
mwachaje
8 years ago

3 THINGS 1 OKUFA SADZIWIKA, MULUNGU SI NZATHU AYI. ANADZIWA NDANI KUTI MNYAMATA NYONDO ANGAPITE KUSIYA WAMKULU PETER 2 FIRST PAST THE POST, NDIMMENE TIMASANKHILA PULEZIDENTI KUMALAWI. AKATI FIRST PAST THE POST NDIYE KUTI AMENE WATSOGOLA NDIYE AMENE WAWINA. KOTERO KUTI APITALA ngakhale AKADATSOGOLA NDI MUNTHU MMODZI YEKHA, AKANAWINA BASI.NDIYE tizindikile kuti kusiyana KWA 36% ndi 27% ndi 9% imeneinali anthu opitilira 400,000. 3 KWA IFE OKHULUPILILA, ZIKACHITIKA MONGA ZINACHITIKA MAY 2014, TIYENERA KUFUNAFUNA NKHOPE YA YEHOVA NDI KUMUPEMPHA KUTI ATIZINDIKILITSE CHIFUNIRO CHAKE Pa MOYO WATHU. TIZINDIKILE KUTI MULUNGU ANALI ndipo ALI NDI KUTHEKERA KONSE KUTI TIPAMBANE, KOMANSO YEHOVA ndi… Read more »

kaya
kaya
8 years ago

CSOs can you provide monetary support to Malawi for the Government to fulfill all the demands you are putting across. By the way which CSOs are these? Can you identify yourself because some of the CSOs are equally surprised and shocked with your demands. Leave the President alone!!!

wika
wika
8 years ago

A viola mumangafuse kuti kodi peter akapanga resigh atenge mpando ndani? olo mwana wa std 5 atha kukuyankhani funso lopusalo. kodi malamula adzikolino suwadziwa? Mwachidule tingoti kayambeninso sukulu[primary}

Read previous post:
Onesimus ridicules non believers in his new song

Through his musical journey he met the Messiah and he was saved. He sings and boasts about Jesus Christ as...

Close