Email a copy of 'Mutharika to attend Sata funeral in Lusaka' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

32 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Zachisoni Phiri
Zachisoni Phiri
9 years ago

Pamalawi apo kukwera mafuta anthu chiwewe akatsika opanda olankhula

Ophee Wa Mbukwa
Ophee Wa Mbukwa
9 years ago

RIP Sata,thnx mtharika jst 4 de sek of attending de funeral,God bless u! but rmemba ppo bhind u,their fate,their taxes u r eating! watch out folks.

NKakosyaga
NKakosyaga
9 years ago

tasiyeni akuluwa apite si kuchisoni kumeneko,za ulendo wa head of state wa ku maliro ndi kukwera kwa mafuta zikugwirizana pati? Mwatani a Malawi,mafuta ayamba lero kukwera simumadya simumakwera zokwera. Ulendowu ndi wa tonse padziko sikwathuyi.

Lange mushy
9 years ago

R.I.P our neighbour president.

GA
GA
9 years ago

Yendani Bwino Mr President..Ife Tizavaya Nawo Pokawaka Chiliza…

Alfred Munduwabo
Alfred Munduwabo
9 years ago

We are asking our good president to send a good number of delegates , Zambia is very near and the president can afford to hire buses and minibuses to escort our president to go and attend The Late Sata Chilufya funeral , he should not worry about the foreign currency , there is plenty of Zambian Kwacha which he can change at Mchinji border.

A Konyani
A Konyani
9 years ago

Yendani mutipeza.Mafuta ndi omwe akwerawa.Tikadapita nanu koma mafuta ake tigula ndi chiyani?

k majola
9 years ago

lets hope Sata is safe, because this is the end of every man, get prepared 1 day it will be u & me have u met ‘JESUS’ B4 YOUR TIME COME

Brainfast Mpoto
9 years ago

i’m sorry wa neighbour nanga ma president azingopitirira ngati ndalama kuika mthumba lobowoka abale,zanazanali anali a Mwanawasa lero ndiawa a Sata,shaaaaaa! ma Zambia tiunikepo nanga ulendo wa a china Kaunda ndi a Chiluwa zinawadutsa bwanji?God bless Zambia.

chishimba
9 years ago

pitani mupeze allowance ife mafuta ndi awa akwera aaa bola a mai zakuba sizingayende munaba ma vote nkumati cha mkwiyo wa Mulungu

Read previous post:
Kanyenda claims brace to inspire Polokwane FC

Malawi international veteran striker Essau Kanyenda on Wednesday scored his first goals of the 2014/ 2015 in the South African Absa premier...

Close