Email a copy of 'Namata, his wife face fresh charges: Malawi cashgate' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

26 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Hameed Chiwaya
Hameed Chiwaya
9 years ago

wanted nane ndikugwilizana nayo mfundo imeneyo maka kuno ku Balaka eeeeeeeeeee kwawonongeka mayi Boaz ndi azinzawo

PS Wamkulu
PS Wamkulu
9 years ago

Ife amene tinadya pakulu tili phee, kumwa wamkwaka!

Titus Skoti
Titus Skoti
9 years ago

Inu a ACB mukuitha ntchito! Keep on purging these parasites called “Accounts Assistants” from the civil service. Timadabwa momwe anthu amenewa amanyadira ndi ma second hand cars from Japan or Dubai. Kuona ena nyumba zomwe akukhala zoposa anthu omwe agwira ntchito m’boma zaka zambiri kuposa iwo komanso olandira ndalama zoposa iwo. Kuba basi!! A Alice Namata ife tinkaona the cars you used to ride osadziwa kuti mukumaba misonkho yanthu pamodzi ndi mwamuna wako. Ife kumadabwa kuti kodi ma PAO amanyauda chonchi pa Capital Hill? But when we saw the other PAOs, they were paupers like anybody else koma inu munali… Read more »

mlaa
mlaa
9 years ago

Malosa boy.

Tunthumbwana tambewa
Tunthumbwana tambewa
9 years ago

Acb yaying’ono yongogwira ana akulu atani mpaka zaka 5 zitha nkhani zosatha. Kazingokalimani msamatipusitse.

wanted
wanted
9 years ago

ACB can you deliberately investigate all district councils esp on LDF funds zikudwedwa koopsa

Biswiki Nyirenda
9 years ago

Namata alibe mulandu apa coz it is only dumbo and dumbo. Pali anthu ambiri sakugwidwa. Like in 2011, someone in the Ministry of Agriculture, a bossy idiot who claims to be professionally IT literate anadzipatsa ndalama kumalipiro ake and because this had been his behaviour, the ministry posted him away. Munthu ameneyu afufuzidwe. He was shielded by a certain PS and that is why he was posted away. Koma munthu ameneyu wazitikita ndalama zaboma kuchokera ku masalary. Khaya, ine ndakamba

Arthur G.M. Mtambo
9 years ago

PLEASE CLEAN ALL GVT SECTORS IN THE COUNTRY THEN PRIVATE COMPANIES FOR THE GVT.

Ralph Kasambara
Ralph Kasambara
9 years ago

I will make sure you are not convicted on this one…dont worry about some of these jealousy Malawians coz they literally own nothing!

Hameed Chiwaya
Hameed Chiwaya
9 years ago

Egritta Ndala mukatha ndi atown mubwere kuno ku BK district council, Agriculture ndiku chipatala kuli ka cashgate yowopsa kwabasi azimayi awa Boaz, Thikiwa, Mzirahowa ndi ena akusakaza chuma cha boma

Read previous post:
Two men who torched ‘witches’ houses in Chitipa jailed for 32 years

The Chitipa Magistrate Court has  sentenced two men Moses Msukwa, 20, and Flackson Masebo, 19, to 32 years imprisonment with hard...

Close